Police in Mangochi have arrested four councilors for stealing money from the district’s council.
According to Mangochi police, they are yet to establish the amount of money the councilors swindled but they are investigating the issue.
Police further said that they will hand over the case to Anti-Corruption Bureau (ACB) once they finish their investigations.
*This breaking news story is being updated, please visit this page again as more details will be published shortly.
If you want to receive all the breaking and latest Malawi news alerts via email, subscribe in the comment box below.
Malawi will not dvlop with dis unbecoming bhvr
dat’s vry unpatriotic
chimangeni basi.
http://shareduty.com/?id=664
Eshhhh
Mbatata yikakula siyiwongoleka. Awa musawasiye akwizingeni, alowe khoti, liwaponye kundende. Awa ali pa school ya Ucashgate, mukawasiyilira mpaka kumaliza univesite yawoyo nde akayamba ntchito yokaba mabilioni ku Capital hill. Akufuna kuti aziti boma lilipoli lalephera kupanga zitukuko pamene iwo akuonongela dala ndalama za ife a Malawi. Uchindere pela. Ving’unu na ise yayiii!!!
Kkk koma zaphweka ndimacounsillor omwe?? Bola tingogawanapo zasalazo basi kkkk
Yapa nde mwauyamba dala unyolo utangokhala pakhoma, akukwidzingeni basi, umbava opusa nawo umenewo. azimanga ogenda chikwangwani nde inu angakusieni?? Mukaisova konko pitani
Kkkkkkkkk koma muli
Malawi 24 we want news and not only about rape,killing and steeling we want goods about the economy
Ndiye apa tizitiso Cash Gate or what Thandizeni guyz
Mbavazo musazitaye zikusaukitsa boma la MANGOCHI.
I saw it coming.
Ana amwachowe, malindi, ntagaluka, ndi malombe siocheza nawo
Kuba kumeneku koma guyz
Malawi yavuta ndikuba mukutichititsa manyazi abale.
Ana oganiza amenewo
Ndakuvera chisoni oba ndalama zochepawe ndikukakhala ku ndende oba ma bilion ali phe kwao
http://shareduty.com/?id=664
Ndibwino nangasi mmati ndi amayi ndi chipani chawo cha PP nanga akubawo ndi a PP? Mwawonatu baza zili m D pwi pwi mwaziona nanga muti chani pamenepo
Amphatso ndiye mwafa makutu,kodi njala kapena. Nankha ati ku machinga tawelengani kachikena kape simumatha kusiyanisa machinga ndi mangochi eti?
ana antcheya amenewo bakili muluzi sons
Ndimadana ndi tianthu timeneti, kaya tinkabwelelanj? Tikungoipixa zikoli basi
Kakolope nyanja mmbale
http://shareduty.com/?id=664
Eat wat u can leav wat u can mmmm n go to przn
Beta Kumangochi Nanga Kucapital Hill? Hahaaa Asiyeni The Big Fish In The Ocean!
http://shareduty.com/?id=664
http://shareduty.com/?id=664
Too much intrest corruption and greedy
Mijomba za wavuta atha nzelu sono,After njala kumalawi eee mijomba imanyanya kuba eeeeee.
iweyo sumabaaaa?
We are waiting to hear more from you
Yaaa ulamulilo ukamavuta ndichoncho iban bas asamatitenge ngati siyanthu tizasiya kuba zikazayamba kuyenda bwino tikhaulitsanapo pano
Ayii!! Awamanga chifukwa apolice sanagayileko ndalazo.
Mwadya 1 anthu akumachinga
Kodi mijomba bwanji Kumeneko? ??
Kodi mijomba bwanji Kumeneko? ??
http://nyimbozathu.com/play_song.php?songID=0.19812300z1455293826
http://nyimbozathu.com/play_song.php?songID=0.19812300z1455293826
http://shareduty.com/?id=664
Ofunika kuwakhoma msomali paliombo umene anawuona a Tcheya wa Solobala..
Ofunika kuwakhoma msomali paliombo umene anawuona a Tcheya wa Solobala..
Mwazichita bwino umbava uchepe
Mwazichita bwino umbava uchepe
Amangidwe amenewo.
Koma kumachingako ndie mwafasako eeee siku ndi siku nkhan yake izikhala ya kumachinga?? Eeee
Koma kumachingako ndie mwafasako eeee siku ndi siku nkhan yake izikhala ya kumachinga?? Eeee
Malawi for sale……negotiable
Malawi for sale……negotiable
deserve jail
deserve jail
We are tired of this,thats why donors cant come in.Ndikumtundako kuli ma loop holes.
ndiye choncho chitukuko chikhalapo
Whats wrong with them? Put them in prison thats all no more stories Dmn
Whats wrong with them? Put them in prison thats all no more stories Dmn
U hv just been elected bt u hv started alibaba , shame on u
U hv just been elected bt u hv started alibaba , shame on u