The Flames of Malawi are expected to start camping on Saturday ahead of their crucial group L African Cup of Nations encounter away to Guinea on 23 March before hosting them at home four days later.
Football Association of Malawi (FAM) general secretary Suzgo Nyirenda confirmed the development but was quick to say the camping will comprise of the local based players only.
“Local players will start camping from 21 February up to 20 March and after that, Enerst Mtawali will name his final squad for the game. We have advised Mtawali to include more professional players because they are the ones active now considering the fact that local players are not playing at the moment,” he said.
Malawi is third with a point, 3 points behind leaders Swaziland. Beating Guinea will revive Flames chances of making it to Gabon but any mistake will surely end their dreams of appearing at the tournament for the third time in history.
Mtawali’s boys started the Afcon campaign on a very bad note after losing 2-1 to Zimbabwe at home before recording a 2-all draw away to Swaziland.
this is a waste of resources, Flames chani, bola netball, chilichonse kuluza…mmmm
Tangotsekulan munda waukulu adzikanjanja ndi khasu anyamata amenewa mwina njala tingamaimvele ku maiko a anzathu
tangogulani ma condom bax ngati ndalamazo mwazikhuta
Ayayayaya mwina ilimba koma pangani zoti tidye amalawi
ready to loose flames
Mbola zenizeni.
Akuti flames za ziii!!!!! nde bolaso netball
No comment
Flames 0 – inayo 4 believe me
yangozisiyani timu idatha imatidwalitsa ikamaluza.
Ligi Inatha Kalekale Nde Ma Players Muzikawatenga Kuti? Inu A Fam Ndondomeko Yanu Ya Lig Muziyendera Limodzi Ndimaiko Anzanu,pano Ma Prayers Ali Ku Chuti
Kunena zoona mukanango siya bora chi team ichi nde mbora yeni yeni.
Flames ndikanyama kanji nthawi zose imangoti tikukoza team tazisiyani zimenezo osangogula grandmilo
Kenako tizizamvanso mwamaliza makobidi mkupanga pull out 4m di tonamenti………
Wasting of tym and money
Mukhale ready ndi ndalama yogulira Panado coz Flames imadwalitsa mutu..
Tizikaluzaso bola ma queens
Inu a flems, mumatha kuonera nawo mpira waazanu inu? Eish manyazinsoo ii!!
mukapange zakupsatu kumeneko osakatichitisa manyazi
osagula mankhwala bwanji ?
Ndekupita ma player ake ati
Kuno Kwathu Kulibe Tsogolo La Football Ndiye Ndalamazo Ndi Bwino Kuthandiza Netbo
Kuno Kwathu Kulibe Tsogolo La Football Ndiye Ndalamazo Ndi Bwino Kuthandiza Netbo
Ngati mukufuna kuti mukawine,Musaiwale sindi simtowe ndi mwawi kumwenda
Lets support the boys in good or bad times.It is a national asset which carries our flag where ever it has engagements.Frustrating comments will only frustrate yourself as an individuale and the entire nation as a whole.Go flames!Go Mtawali!
Makape,
Angotumiza Noma
Shaaa! Mitu ipwetekenso
bola flames yachina P. Mponda inafikako ku AFCON, koma iyi ndiye kubetsa ndalama.
Eish ayambanso za fulemuzi za ziii!
Mwat flamez bola queens.
just go into camp a week before the game to save tax payers resources
azipanga camping osadya ngati ku ma hospital.
Amalaw tisagwetse mphay mapleya komaso coach kut sitikawina mmalo mwake tiwalimbikitse. Pamene pali vuto tiwauze mwina nkukonzapo mwansanga kut kumeneko tikachiteko bwino. Kod timu ikaluza amamva manyazi nd kochi yekha kapena dziko lonse? Amalawi why?
Mukamasankha squad yanu please include Mwayi Kumwenda,we want more goals please
Mukamasankha squad yanu please include Mwayi Kumwenda,we want more goals please
kukakwapulidwaso
Ndinjala ndi njala osadya angakawine!
Apapa akufunika angotenga bullets kt ikadode basi cuz flames inatha
Bola Kut Isewere Bb!!
ZaGanja basi
Zaziiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii
Osangogula chimanga dollarzo bwanji kukapasa anthu akumuzi bola mukanati nkhonya kapena netball tikhoza kupindura
why camping with players who u know will not be used?we already heard that Ernerst is going to use foreign players.
ipite tikazionere konko
Tangotumizani ma timu ya azimayi ija ndi imene ife tikuyidziwa osati agwaladiwa
flames of malawi?
Fitness ndiyedi palibe vuto lina kwathu kumo offseason ndiyaitali kwambiri 4 months? kumakhala kukokera ndalama or bwanji? Minyendo yazizira ma players
ikadalipo?
Osaononga ndalama ndi flames nthandizani anthu akufundinjala palibe chomwe anga chite.
Mxiii
Ngati zenizeni
Azatichinyeso eish!!
Moto buuuh!!
Nawenso flames osangokana bwanji??
zachamba
mm guys ine tmu yanga ndili nayo,frames yanuyo pitanayo ni uko yati dyetsa udzu thawi yaitali== =nyerere the nomads!
waste of time use the money u wasting to buy more maize…just give up amalawi mpira unatikanika basi iya
Football needs fitness and good timing. Malawi National team lacks good striking force and midfielders.
Aaa, si mavuto okhaokha amenewo?
Atleast this tym do something better
BB moto kuti buuuuuuuu
Amabungwe amangodziwa kulesa zinthu zochitika koma kuti athandizile kulephelanso.