Mayor of Malawi capital, Lilongwe Council Willie Mayor Chapondera has said that the council is seeking a lasting solution to the problem of street vending in the city.
He said street vending has for a long time been a problem for the council and they are planning to hold a meeting this week in order to address it.
”We are expected to hold a meeting with other councillors in order to find solutions to the problem,” said Chapondera.
He added that vendors had been adamant to leave the streets even though the council built a temporary market for the vendors to sell their goods in.
”Despite our efforts to end street vending by building a temporary market, vendors choose to sell their goods in the street and when police come they run away and return when they are gone,” he said.
However, Chapondera admitted that the council had failed to end street vending that is why they will hold a meeting to find real solutions together with other councillors.
For a long time government has been making strides to end street vending but most vendors had been adamant as they continue selling in the street despite having markets.
A Mayor a lilongwe ndi agogo ndiye zoti dziko likusita ili sakuzidziwa
A Mayor a lilongwe ndi agogo ndiye zoti dziko likusita ili sakuzidziwa
lack of job opportunity its what makes pple 2 engage in illigeal vending
Asiyeni atakate inuyo mukuona ngt azikadya kut
Aha! Kodi mzinda wa lilongwe uli ndi mayor!? eish
RSA mavenda ndiosayamba ndiye Malawi ndikachani? Akupatsanidi mutu wa ching’ala ng’ala simunati.
Does Lilongwe have a Mayor?? like,seriously??
Bas azingopanga yomwe anzawo apanga ku limbe zana. Vuto ma fares a mumsika ndi odula much nde nzovuta kut zizathe.
Umbava ukura chonde
Yambani mwa chotsa ma thankala pa injena Ku kanengo near kanengo Police Moto Moto mera inalephera
Palibe dziko lopanda mavenda koma bcz of the stupid of Malawi thats why ,koma mavenda amathandiza kwambiri anthu osauka powagulitsa katundu,zakudya pamtendo wotsika
Ngakhale kuno Durban South Afrika anthu akugulitsa malonda m’misewu kd kumalawi kwatani#SANJE BASI ZAUSILU
akuba athamangiseni anandibera ndi tabemwera ku malawi pa holiday
Limbe allso
Vendor ndi vendor basi
Mr Mayor, try to source enough funds to construct many tall infrastructures, and construct roads, put shades at the minibus ranks, build good pay toilets,,(you will make money) , and make sure all Malangalanga roads are tarred …advice shop owners to renovate their buildings and add some two or three floors up…that will make Lilongwe a beautiful city. All buildings along the roads must be tall…Make a good plan Mr Mayor should you want to make the city beautiful …Stop wasting resources in hiring armed forces to fight street vendors ..
And kwa mavenda,, chonde, yesetsani kukonda town yanu komanso kuyiteteza…sungani bata …..monga mseu wochokera ku bus depot kumalowera ku depot ya ma minibus,,, mumayala mmbali mwa mseu mmalo moyala mphepete mwa mpanda uja …pemphani ku city council mupange ma bench olongosoka mudzigulitsa.
Zikomo.
No they can do that in town not cicy centre its everewhere to vend jozi the good example
Why?
iwe uku lephera kukoza town yalilongwe kuti izioneka ngati capitalcity nchito kulimbana ndi Ma vendor basi koma iwe kamba ina
remove the debris and make the city clean
Ndiuzeni town yopanda mavenda my Africa mupeza kuti ndi halare ndi ena ma twn amu zim yokha basi yomwe boma lake they don’t care about peoples lives,,
Muwachose misewu ndi anthu akuba amenewo
Ku America iliko ndinagulaso chimanga chophika panja pa shop ku Durban natal,pa mesinaso pali ti maokala osati mashop
Eeeee zotsatira zaizi amatsekulira masoldier chifukwa apolice amachepera kaba ndimavendor Army ndi imene imateteza nkhani yamavendor
Iiiiiiiiii vuto lake sionse mavendor ali abwino kapena oipa iiiiii asova
Njala imeneyi mukulimbana ndo vendor zausilu
Street vending its not illegal
as far as l know a #vendor that headache will lead to #heart_attack
Kaya
tikhala tikugulisa mmenemo mpaka kale lol…
Street vending ili ponse ponse.maiko olemeranso ziliko