Malawians loitering in SA

Advertisement
Lindera camp

Huge numbers of desperate Malawians have been seen idling around Lindela Repatriation Centre in South Africa after being released from the centre.

Malawi24 understands that the South African Government has stopped deporting Malawians saying that it has no funds to carry out deportations.

Lindera camp
Malawians loitering in SA.

However, authorities in South Africa are still arresting Malawians and people of other nationalities who are living in the country illegally.

Once they spend six months at Lindela Repatriation Centre, they are released and dumped around the facility.

One of the Malawians released last week after spending six month at Lindela, Thabiso Phakati, shared his story with this publication.

“I have seen my fellow Malawians around Lindela desperately begging on the streets, they have no any other option,” he said. “I saw women just crying outside Lindela, when you are in Lindela you receive meal once a day.”

Late last year, government said it had repatriated over 2000 Malawians who were detained at Lindela while other detained Malawians made their own arrangements to come back home.

Advertisement

394 Comments

  1. ZAZII. ALIYENSE NDI WAMKULU. AMASANKHA YEKHA WHERE TO STAY AND WHAT TO DO. WHO ARE YOU TO JUDGE. ANTHU AYAMBA LERO KUYENDA? MIGRATION WAS THERE, IS THERE AND WILL BE THERE. PAMENE WINA AKUONA BHO WINA AMAONERA MWINA YOU CAN’T ASSUME SOMEONE IS CRAZY COZ THEY WANT TO TRY SOMEWHERE ELSE. NDIYE UMBULIWO.

  2. Onyoza inu teroni koma Chomwe mungadziwe,theba sinama bapangani phokosolo anzanu tikusuntha komanso ngati theba uno kuli anthu amene amakhala malo abwino ndi obwera ndiye tiyeni bapangani phokoso ife tikusuntha pomwe inu udzatenge mukhala nawo mpaka kale (khalirani kuthira mchere mu ndiwo tidzakumana pa kachere).

  3. A malawi24 penapake taziganizani ,munthu anagwidwa Ali ndipokhala,lero wamasulidwa ndiye azingoyendayenda osalondola kumene amakhala. Bodzatu ili

  4. ine nde olo mutatokota bwanji
    sindingayelekeze kubwela kumpanjeko
    kuno ndikuva kukoma kwambili
    inu bagwilan maganyu oumba zudinawo kkkkk nanga ganyu wa 4000 mpaka one week ukanagwilabe
    kuno tikufila ntendele ifeeeee

  5. Kwathu ndi kuno ku M,alawi ndipo takulira komwe kuno koma zowoona zake bola maiko ena osati kuno anthu andale ndiwo akupindula

  6. Never ever will i think of going to Nyasaland,am done with that country,its like a cursed land that does not bear good harvest

  7. Ku SA ukapitirako umphawi wakwanu ku mtundu wakwanu nde suuvutika pobwerela kumudzi koma mukapitira kunjoya nde hmmm ndi zija amabwera opanda kalikonse kochepa mukupezako anthu aku joninu zithandizaniko akwanu kut mudzapeze pofikira zikadzakuvutan

  8. Amene akumva kuwawa kuno, ndibwino azivaya pa malawi. kuno ntchito ndizosiyana, ndie ngati winawe unapeza yowawa zivaya uzikalima mpilu or fodya. Iwenso uli kumalawiwe ngati uli ponona usamakambe zausilu, uzawona polekeza

  9. Amene akumva kuwawa kuno, ndibwino azivaya pa malawi. kuno ntchito ndizosiyana, ndie ngati winawe unapeza yowawa zivaya uzikalima mpilu or fodya. Iwenso uli kumalawiwe ngati uli ponona usamakambe zausilu, uzawona polekeza

  10. Anzanutu awamanga ku Mulanje atabwelasa katundu wakuba Ku Jonzko samalani mukutiipisila mbiri,komaso anzanu akabwela kumeneko mukadziwa kuti alinkanthu mpaka mmalawi nzanu kumupha think about it

  11. Anzanutu awamanga ku Mulanje atabwelasa katundu wakuba Ku Jonzko samalani mukutiipisila mbiri,komaso anzanu akabwela kumeneko mukadziwa kuti alinkanthu mpaka mmalawi nzanu kumupha think about it

  12. Speechless watch yo mounth u Malawi 24 to catch the flies just send one of yo family here @sa ihope he/she wil never come back there in Mw mmbiteeee…

  13. Ngati mwati ku SA zinthu zikuyenda nanga bwanji Jocob Zuma wasintha Nduna ya za chuma angati within a short period of time?I just want to remind u all last yr,u know what had happened they wanted u to have more katundu so that adzakuukileniso akubeleni mwaiwala kale eti enanu simunagone Ku stadium inu? GOD is watching at u

  14. Though there are alot of problems here in malawi but still we are surviving. U can not call your father stupid bcoz he is poor and runing away in yr on house. why can’t u find solution to that problem while u are there.

  15. I’am here to blame Malawi24. Plz you must confirm be4 you update your fucken stories. Of cause those who were in Lindela ‘ve released but it’s not in such situation as you are saying. Some of them are now in their working areas as here in Durban tilinawo kuno anafotokoza momwe zinalili. Nkhani zokhudza kuno ku SA zisiyeni as a result mudzapangitsa kt anthu anu amene tilikuno ku SA tivutike zenizeni akunowa akamaona nkhani ngati zimenezo.
    You are forgetting that some of Malawians akuthandizika from their fellow relatives who are in SA. As of now ku Malawi tikudandaula kt kuli mavuto osiyanasiyana monga azachuma, njala mongotchulako ochepa. Now kupezeke kt mtundu wa a Malawi ulikuno tikadzazane kumeneko….! Mavutowo angzafike pati? Sindinathyole m’nkhwani, ndangodutsa chabe…..!!!

  16. Amalawi ena ndi zitsiru ndithu chomwe mukumanyozela kwanu kokongola kopanda nkhondo ndi chiyani, koma penapake sukulu ndi ya bwino i knw most of them sadapite ku sukulu ayi ana amagomo osadziwa ndi nkhuku yomwe mbava

    1. Malwi remain the poorest country in the world aliyense amaziwa kale zimenezo nde ife tisiyen tili ku jons kuno ma passport tinapanga tokha transport nde #tjoo enanu tikudziwa ndikulila ndi mtima kuti simuzaonako bas but sorry ndinthawi ndipo zoti kuli zokhoma ai ndithu musamavutike timathamanazo tokha ngati zikukuenderan #satanic zanu mwayamba kumalawizo ndizanu koma palibe kupangira mwina we’r still here in jons ngat kubanja kwa2 kumaoneka kusitha haa nde munthu wake ndineyo ndithu ndilama zakenso szakumalawi kwanuko aa za jons mukunenayo enafe tikuimva bwino ndithu #mxxm #stupit

    2. ZAZII. ALIYENSE NDI WAMKULU. AMASANKHA YEKHA WHERE TO STAY AND WHAT TO DO. WHO ARE YOU TO JUDGE. ANTHU AYAMBA LERO KUYENDA? MIGRATION WAS THERE, IS THERE AND WILL BE THERE. PAMENE WINA AKUONA BHO WINA AMAONERA MWINA YOU CAN’T ASSUME SOMEONE IS CRAZY COZ THEY WANT TO TRY SOMEWHERE ELSE. NDIYE UMBULIWO.SUKULU YANU SIMUNAPINDULE NAYO.

  17. Changa ndichisoni kwa omwe akunyoza dziko lawo. …kumalawi ndi kwabwino ukakonzekera koma ife amalawi ambiri tiri moyo oti tazipezelanji……..nkhuku zomwe zikunenedwazo ndi free range tu pamalawi. …..ufulu tikunyadira kunowu dziwani kuti eni ake anauvutikira……..tiyeni kumalawi tikamenyele nkhondo dziko lathu ….nthawi ndiomweyi yokadzegula ma ptc

  18. Der is no such thing lyk Malawians are suffering in or near Lindela,Get facts first n den wena stupid cying ukuth u r going to beat foreigners up uyi silima ndoda Nelson Mandela must b turning in his grave

  19. Amanga kuphela Akulanto eyokuthi abantu baseMalawi bayahluphekha elindela mina ngihlala maduzana kulendabo.Masizwane bafethu, ma ukuthi alisela ndaba eyokubala emaphepheni kungcono lihlale emakhaya cz wat u the so-called news24 Malawi are updating Abig SHIT!!!!

  20. Home is best, even Kamuzu came back after a long time. Mipaliro ndi zibonga zama Zulu ikazayambiranso, muzalalaka kubwera kumudzi kwanu, Malawi mudzamuona ndi maso koma simudzamfikira. Musaganize kuti ma bus boma limkatumiza aja azabweranso kuzakutengani nthawi imeneyo idatha nayenso tili pa mabvuto. Rand nayonso ikungogwa ndiye musatinyoze ndife abale anu. Palibe amalandira R5000.pamwezi kumeneko. Ntchentche inati mmbuyo mwabwino mtsogolo mwabwino.

  21. Chikumbutso zidana naneso ndinali phunzitsi kumalawiko ndikudziwa zakuwawa chifukwa ndiwe Aphunzitsi pano ukulandila zingati?dilu yamabuku ilipo nanga choko kkkkk?

  22. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

  23. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

  24. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

  25. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

  26. Dnt take advantage to talk nosense..enanu mukuthawa ngongole, ena mudasya mimba kuno..what ever the case, malawi is ua root.akayamba kkumenyani dnt seek help from our government..ife tkuphunzira momuno,,kudya ndkupeza ndalama momuno en we’re still survive..

  27. Simukumachedwa kupsya tonse tinjinga kugulitsa,tima dvd,tima screen ashame of u don’t forget that u Malawians OK,muzatipeza kwanu mkwanu mthengo mudalaka njoka

  28. Home is home though it never be so homely. When xzenophobic attacks erupt, you will be back.

  29. Amalawinso Apa Alemba Kuti Muli Desperate Ku Joni!Komanso Mukunyoza Amzanu Kuno Mukupindula Chani?Akatero Ayambe Kukudulani Makosi Zeno!

  30. Always loosers give up,u gave up for ur country but wen ur chased with xeno u wanted our taxes to offer u buses to come home we only did that out of love but be ashamed of urself,anzanu kumalawi konkuno tikumwera 30 thousand aday inu kumalephera kuipeza kumeneko hence forth ati alikujoni shame!! Osangobwerako bwa muzizadulansokho mulemeletse dzikolanu.am jst sick of u guys

    1. Hey man musalankhule mokuthamau cozy enafe timachoka mafamily ovtika mot KT a2 adye akudalila ife ndye musamalankhule ngat a2;otse Atari abwere kumeneko mungawapatse zochita ine2 ndinali komweko last DEC a2,akvtika kumeneko iwe omwera30 osawathandiza bwanj mind ur mounth broy

    2. ZAZII. ALIYENSE NDI WAMKULU. AMASANKHA YEKHA WHERE TO STAY AND WHAT TO DO. WHO ARE YOU TO JUDGE. ANTHU AYAMBA LERO KUYENDA? MIGRATION WAS THERE, IS THERE AND WILL BE THERE. PAMENE WINA AKUONA BHO WINA AMAONERA MWINA YOU CAN’T ASSUME SOMEONE IS CRAZY COZ THEY WANT TO TRY SOMEWHERE ELSE. NDIYE UMBULIWO.

  31. Guys tisamaname munthu amene amalandira K200000 kumalawi ndi graduate pamene ife timaipanga pa week zikungofunika dongosolo basi lamapepela otherwise me am here to stay

  32. Those of you who have not been to South Africa can be cheated.They sleep in tin houses chigulu which house are you referring to? The type of work is tennantship or another slavish work

  33. He he he Joni ndi imodzi koma kusiyana ma film…enafe konkuno timayendera njale za nyatwa, nyumba za bho, ndalama sinkhani komanso a police kapena a home affairs ndi amzathu ndipo sitimawanyumwa popeza mapepala okhalila kuno tili nawo.
    Zimangofunika ndondomeko zinthuzi abale.

  34. Mukhale ku South Africa konko musabwere kuno ku Nyasaland ayi mabvuto ali kuno timawakwanisa tokha inu simungamake DZIKO lonseli mwini wake ndi MULUNGU.

  35. being in S.A for 10 years now and this is my home as well. they can deport me but I will come back again. kwathu kunalowa mbola besides when u doing better mmm too much jealous.

  36. Ndikatan ku malawi nkhuku nkudya dairy no matter what never go back to malawi koma na ine ndi akubanja anga tagwirizana zokhala kujonz kaya tiliman chöncho mukalamba nsangamuona

  37. Zoonadi ena ambili atulutsidwa,masiku 4 apitawa,mmodzi mwa azibale anga awiri omwe anagwidwa 4months ago wabwerera kunyumba kwanga,zili bwino ndithu,sitibwera ku mpanjeko unless mutapha wamathanyulayo kaye,finish.

  38. kwathundikwathu tazabwelela nthawi ikwana osati pano aliyense akufuna kuchitabwino palibe mnthu angavomele kuti azikhala ovutika padziko lapasi ndyeno nafeso tikuyesesa pamphavu zathu chifukwa chonenepesa hkhumba cchiziwikatu kusiya ndikungokha pakhomo akutitu kobwela kokha kamalaula sichoncho ndiposo akuti pofela salambula

  39. Home is best ever,,,i am also here in SA Midrand Joburg, but even rand by now is drown heavy and food rent are are very expensive. If you can count down all that,, you better make business home or work and get paid mk50 000 but you stay at your home. 85percent malawian are getting that peanut. Lets not to our fellow malawians. They will not welcom us after we go home with nothing. Luck me i did what i came here for and increase wth others. But i still do not have money. South africa is good to those who know hand works. Chilungamo sichiposa apa,,amalawi ambiri amagona mu mikhukhu yoti ngati mmagona nkhuku kamba kosakwanisa ma kulipila room. Room ya one bed ndi r700 above=mk30.000. Food r450=mk19,000. Nde umalandila mk100,000 ukhala nd zingati? Uchoseso transport. Tiyeni tizinene zoona kuti, bola poti pamwezi timapezako kusiyana ndi kwathu.

    1. Iwe nde m’malawi owumira, chakudya R450?? Even in mikhukhu almost them as sell stay in them, not only malawians. Stop just raising nosense points my bro. Kumaganiza, ngati iweyo umalandira kochepa it doesnt mean all

    2. Most of south africans are staying in mikhukhu, and amalolera nyumba kupangisa rent kwama foreigner omwewo iwo azikhala mumikhukhuyo stop making us mad

    3. usaputsitse anthu ada,ngati pali omwe akukhala ma nyumba abwino ndi ma foregners,……anowake amakhala mikhukhu nyumba yabwino kuyikamo a rent,may b ndifunse uli dera liti?Coz SA ndiyonse koma kusiyana madera.Lilongwe ndiyonse koma ena ali kwa msiriza ena ku 25 ena kwa mgona,iwe SA uli kuti ?

    4. Aise fundo yomwe wanenayi ndiyowo, and ineyo ndikuvomereza kut S.A. siri mwakale. Even ainuwake akudandaula kut zithu zikuvuta. Mbuz zomwe zikulesazi ziribe dzeru ndipo kuno anabwera opanda cholinga, amangoti bola akudya nkhuku.

    5. Kubali ya magonedwe apo ndiye wanama, Amalawi ambiri amagona ma room. Angakha tikuvutika komabe timapeza kenakake. Pali anthu ogwila ntchito m’boma almost 5yrs koma angakhale DVD Player alibe.

    6. Tiyeni tizimva kamodzi, nkhani ndiyoti boma la SA ilibe ndalama zotumizira ma foreigner osati zachamba ukukamba apazi ayi. Kwina kulikonse zinthu zikudula potengeranso ndimmene ndalama yawo ikuyendera. Nanga osamangopita bwanji muzikagula zochipazo? Nenani zamavuto anu osati wina aliyense ayi. Oky ndigulu lija loti mukapita kumudzi kumakathoka za anzanu aja etiiii.

    7. Ngati iweyo ndiwe wa garden service dnt think everyone is. Learn to speak for yourself. Osamati tikulandira peanuts wamva? Bwanji osangokhala phe ngati ulibe chonena chanzeru

    8. Nkhani ndiyakuti,,ngati ku MW ukuteyesako kukapeza ka khobidi,,pitiliza kaye zomwe ukuchitazo. Ngati watha ma plan, bwela kuno uzazionela wekha. Zakuno sauzana mwayi ndiosiyana

    9. hahahaha come to capetown suzalandira pin ukunenayo,,,and amene akugona mmikhukhuwo uwone zomwe apanga kumalaw ndizot sakanakwanisa ali konko kkkkkkkkkkkkkkk

      1. kkk, enatu kusayendaku sichina kufuna kumangothirabe mchere mu ndiwo ku kitchen ,dikuzolowera kukhala mu nkhhwapa mwa makolo awo, asiyeni atokote ife zathu zikusongola

    10. Ku cape town kwatani iwe? SA is SA. And kunoko panopa tangozazana ngati nkhuku. SA panopa yaonongeka chifukwa ndi dziko lomwe kumathawila mbuli. Nde akamati ndizikulipili r1500 akungovomela. Yet akusungidwa ndi munthu, munthuyoso ali ndi mavuto. Honest will always set us free. SA is not that SA people were talking about yesterday. It is completely different.

    11. Different job with diff salary it matters wat u do n the skill u hv even here life its hard things is hard let’s accept but we need to aim high ena agula magalimoto ena manyumba even here or there but it deppends ndi ntchito yake

  40. Once again,akuluakulu ku SA chonde kuno zibwenzi zanu zikuvuta kumatipempha ndalama daily chondechonde mukalandila ma randwo muzitumiza pena tikumachita manyazi mkumangowathawa take knot that pliz

  41. Dont come to Malawi guys. Education is for poor people. Business for crooks. Nothing is good here! Continue staying in diaspora

  42. President Peter Muthalika ndi boma lake wakhazikisa kale thumba la ndalama kuti athandize mzika zomwe zili ku #LINDELA.president Peter wanena kuti kuli bwino athandize mzika zimene zikuvutika ku south africa kusiyana ndikuti ndalama agule chimanga kuti anthu athandizike.komanso mene ndikuwonela amene ali ku Lindela akupeza mtendele wa dzawoneni kusiyana ndimunthu ali ku mpanje amene akugwila job daily.ku Lindela tea ndiwamkaka.pogona pabwino.kulibwino ndikhale ku Lindela kusiyana ndikupita ku mpanje

  43. We r all human beings take care of urselves en Malawi is ur Country basi even u stay longer but u r a Malawia,a good example Bushil

  44. Sindingabwere ine kumeneko ndidzidzalandira K40 000.00. Pamwezi ndalama yoti ndimalandira after 7 days. …..never adzachoke kaye bwampini ndidzabwera otherwise life is good here timadya bwino, kuvala bwino everything is affordable

  45. God is power,, its nt gud to go back home while u r nt well prepared coz Malawi nw is full with hard problem z,,,ndalema navo mweee,njala too much

  46. Any country there’s deportation! Y b surprised? 2 b @ Lindela doesn’t mean u r a stupid, but u hv no proper permits documents! I hv bn 3 tyms @ Lindela but still now am in S A! Shame 2 stay the so called Malawi!!

    1. God blessed any country on earth n God loves anyone N God gave us brain to guide us to know what we can to improve our lives! There’s enough minerals in MW that can develop the country! The problem is ppo hu calls themselves leaders r not qualified 4 that job! They r qualified only for stealing Gvnt money but not to develop that poorest country! We only need gud leaders thats all

    2. God blessed any country on earth n God loves anyone N God gave us brain to guide us to know what we can to improve our lives! There’s enough minerals in MW that can develop the country! The problem is ppo hu calls themselves leaders r not qualified 4 that job! They r qualified only for stealing Gvnt money but not to develop that poorest country! We only need gud leaders thats all

    1. Ndalama zake ziti kumalawiko.simukudikira kuti muyambe Kaye kukwerana amuuna kapena akazi okhaokha kuti mupeze chuma.don’t count the currency if malawi with rand compare it with the dollar or pound uwonedi kutino malawi Alibe ndalama.

    2. Zili pa Malawi amwene; kuti upeze ndalama zogulira zipangizo zomangila nyumba pa cash? pokhapokha wayenda njira ina yake osati yachilungamo ndi Malawi amene timamudziwa matsiku ano ‘chiphazi’ @ Japhet Chitatanga

    3. Mukamabwela mumatenga ma amplifier ma home fieter ma dvd player kuzatigulitsa opanda ndalamafe pali nzeru zomwe mumabweletsazo kununso ndi zambiri komanso zotchipa

    4. ngati kuno kumalawi tilibe dollar,timabulangete tanu amakugulani ndani? by the way we pay doubble price katundu ochoka ku RSA.

    5. Tiye nawo mudzibwela ndi ndalama osati tima dvd player ndi tima tv screen kudzatigulitsa anthu opanda ndalamafe ndalama zake ziti zochita kusenza pamutuzo 10 yrs chobweletsa tima dvd basi

    6. Kkkkkkkkkk hear yourself! While tikugulabe nyumba za millions zoti inuyo sumungathe pokha pokha mkhale ndi business ya ziwalo za anthu

  47. When ur staying in Mzansi u must have a friend or a close relative so u can’t be desperate when ur released perhaps these guys had their lodgings where they dwell wìth friends or family members before they were netted,obviously in circumstances like this they’ll go back to their folks.Don’t tell us lies.Just tell us that Rsa gvt release illìgal foriegners from repatriation camp,thats all. No foriegn man dwells in the street or under bridges

  48. Timaoneka ngati opusa akagwira amakusiitsa katundu nthawi zina ndalama zako ku mabank komanso mwina kwamzungu zoti wagwira mwezi onse salary sadakupatse mzungu thats why ndianthu odyelera amenewo

  49. zateremu apitilizabe kutigwirako?hahaha ndidyeno Volosi ndi Iwisa mtima uli mmalo kakakaka Ng’iyaithanda londoleyo.

  50. I will never go back to malawi though home is gud whats the use of being educated and receive peanuts southafrica is anice country its amatter of getting the right documents before ucome life is gud here guys

  51. i think we must go back home amene tikusaukisa ziko lamalawi ndiife tili moyenda chifukwa nzeru zilo mwaife amene tikumachoka mmalawipo lupita kwina

    1. Ukunama iwe ine bwanj ndmavaya kenya n south Africa bwanj xkuyenda ku malawiko chmene ungadziwe amadalitsa nd mulungu mu njira xosiyana pali ena ku malawiko anangobadwa kumudz osapitako even mtown koma mulungu anadalitsa nd chuma

    2. zoona braz nanga halfvya amalawi ili moyenda ndichilungamo chimenecho anthu oti alamule ziko lija amalephera kusankhidwa kamba kaife tili moyenda fe.mavoti athu akufunika kwambiru

  52. vyako ivo,kweni picture iyo nja population iyo yikawa kulindela nyengo iyo,Coz this picture is old hope u get from google,uleke utesi admin nizakubafula uheni chomene

  53. Kkkkkkkkk jozi its where we belong for now. Not for ourselves but to make our malawi better as well. We only need chance to get wat we want then we will silently go back to our malawi

  54. Kkkkkkkkk jozi its where we belong for now. Not for ourselves but to make our malawi better as well. We only need chance to get wat we want then we will silently go back to our malawi

  55. Useless people I gather a certain person is arranging to go back who was transported by Malawi Government back here.Never bring them back again they are the lazy group and nomadic leave them to find their own way out

  56. Useless people I gather a certain person is arranging to go back who was transported by Malawi Government back here.Never bring them back again they are the lazy group and nomadic leave them to find their own way out

  57. Life is gumbo as we gumbling here until Malawi adzakhaleso wabwono ngati mmene analili kale mukadzachotsa that gay President we r coming,kuti gwila lero mawa kubweleranso

  58. Life is gumbo as we gumbling here until Malawi adzakhaleso wabwono ngati mmene analili kale mukadzachotsa that gay President we r coming,kuti gwila lero mawa kubweleranso

  59. Kkkkkkkk koma mmalawi sadzatheka basi kulephela kuku otchani ndi moto koma osamva kkkkkkk koma kukhala mmalawi ndikowawa

  60. Kkkkkkkk koma mmalawi sadzatheka basi kulephela kuku otchani ndi moto koma osamva kkkkkkk koma kukhala mmalawi ndikowawa

  61. Bodzatu ili panopa ticket ukumadula wekha yobwelera kumudzi apo bii amangokusunga konko koma zowatulutsa anthu kulindera ndiye sizoona amwene mwanama eish

  62. Bodzatu ili panopa ticket ukumadula wekha yobwelera kumudzi apo bii amangokusunga konko koma zowatulutsa anthu kulindera ndiye sizoona amwene mwanama eish

    1. SA is our second home,amati atani,…….wina umasangalala kumudziko ukamaona anthu akupangidwa d-po-t nde ukomokatu zatha kulibenso ingogulitsa mundawo uzibweera kikkk

    1. Umapitilanji kuziko lopanda chikondi, osapita mayiko enawa bwa? John bas umaiziwa? Uluka ubwele kuno tizavutike tonse. Ife tinazolowela ase uziwona, kunonso tilibe transport ngati tikusowa mankhwala muzipatala, ukuti chani?

  63. This matter should not involve government because these are people who do not have guts as they preferred to stay in the Rainbow nation when their colleagues were being repatriated back to Malawi. Mukhale konko after all we have a lot of financial problems here.

Comments are closed.