Malawians loitering in SA

394

Huge numbers of desperate Malawians have been seen idling around Lindela Repatriation Centre in South Africa after being released from the centre.

Malawi24 understands that the South African Government has stopped deporting Malawians saying that it has no funds to carry out deportations.

Lindera camp

Malawians loitering in SA.

However, authorities in South Africa are still arresting Malawians and people of other nationalities who are living in the country illegally.

Once they spend six months at Lindela Repatriation Centre, they are released and dumped around the facility.

One of the Malawians released last week after spending six month at Lindela, Thabiso Phakati, shared his story with this publication.

“I have seen my fellow Malawians around Lindela desperately begging on the streets, they have no any other option,” he said. “I saw women just crying outside Lindela, when you are in Lindela you receive meal once a day.”

Late last year, government said it had repatriated over 2000 Malawians who were detained at Lindela while other detained Malawians made their own arrangements to come back home.

Share.

394 Comments

 1. ZAZII. ALIYENSE NDI WAMKULU. AMASANKHA YEKHA WHERE TO STAY AND WHAT TO DO. WHO ARE YOU TO JUDGE. ANTHU AYAMBA LERO KUYENDA? MIGRATION WAS THERE, IS THERE AND WILL BE THERE. PAMENE WINA AKUONA BHO WINA AMAONERA MWINA YOU CAN’T ASSUME SOMEONE IS CRAZY COZ THEY WANT TO TRY SOMEWHERE ELSE. NDIYE UMBULIWO.

 2. Onyoza inu teroni koma Chomwe mungadziwe,theba sinama bapangani phokosolo anzanu tikusuntha komanso ngati theba uno kuli anthu amene amakhala malo abwino ndi obwera ndiye tiyeni bapangani phokoso ife tikusuntha pomwe inu udzatenge mukhala nawo mpaka kale (khalirani kuthira mchere mu ndiwo tidzakumana pa kachere).

 3. ine nde olo mutatokota bwanji
  sindingayelekeze kubwela kumpanjeko
  kuno ndikuva kukoma kwambili
  inu bagwilan maganyu oumba zudinawo kkkkk nanga ganyu wa 4000 mpaka one week ukanagwilabe
  kuno tikufila ntendele ifeeeee

 4. Never ever will i think of going to Nyasaland,am done with that country,its like a cursed land that does not bear good harvest

 5. Ku SA ukapitirako umphawi wakwanu ku mtundu wakwanu nde suuvutika pobwerela kumudzi koma mukapitira kunjoya nde hmmm ndi zija amabwera opanda kalikonse kochepa mukupezako anthu aku joninu zithandizaniko akwanu kut mudzapeze pofikira zikadzakuvutan

 6. Amene akumva kuwawa kuno, ndibwino azivaya pa malawi. kuno ntchito ndizosiyana, ndie ngati winawe unapeza yowawa zivaya uzikalima mpilu or fodya. Iwenso uli kumalawiwe ngati uli ponona usamakambe zausilu, uzawona polekeza

 7. Amene akumva kuwawa kuno, ndibwino azivaya pa malawi. kuno ntchito ndizosiyana, ndie ngati winawe unapeza yowawa zivaya uzikalima mpilu or fodya. Iwenso uli kumalawiwe ngati uli ponona usamakambe zausilu, uzawona polekeza

 8. Anzanutu awamanga ku Mulanje atabwelasa katundu wakuba Ku Jonzko samalani mukutiipisila mbiri,komaso anzanu akabwela kumeneko mukadziwa kuti alinkanthu mpaka mmalawi nzanu kumupha think about it

 9. Anzanutu awamanga ku Mulanje atabwelasa katundu wakuba Ku Jonzko samalani mukutiipisila mbiri,komaso anzanu akabwela kumeneko mukadziwa kuti alinkanthu mpaka mmalawi nzanu kumupha think about it

 10. Speechless watch yo mounth u Malawi 24 to catch the flies just send one of yo family here @sa ihope he/she wil never come back there in Mw mmbiteeee…

 11. Ngati mwati ku SA zinthu zikuyenda nanga bwanji Jocob Zuma wasintha Nduna ya za chuma angati within a short period of time?I just want to remind u all last yr,u know what had happened they wanted u to have more katundu so that adzakuukileniso akubeleni mwaiwala kale eti enanu simunagone Ku stadium inu? GOD is watching at u

 12. Though there are alot of problems here in malawi but still we are surviving. U can not call your father stupid bcoz he is poor and runing away in yr on house. why can’t u find solution to that problem while u are there.

 13. I’am here to blame Malawi24. Plz you must confirm be4 you update your fucken stories. Of cause those who were in Lindela ‘ve released but it’s not in such situation as you are saying. Some of them are now in their working areas as here in Durban tilinawo kuno anafotokoza momwe zinalili. Nkhani zokhudza kuno ku SA zisiyeni as a result mudzapangitsa kt anthu anu amene tilikuno ku SA tivutike zenizeni akunowa akamaona nkhani ngati zimenezo.
  You are forgetting that some of Malawians akuthandizika from their fellow relatives who are in SA. As of now ku Malawi tikudandaula kt kuli mavuto osiyanasiyana monga azachuma, njala mongotchulako ochepa. Now kupezeke kt mtundu wa a Malawi ulikuno tikadzazane kumeneko….! Mavutowo angzafike pati? Sindinathyole m’nkhwani, ndangodutsa chabe…..!!!

 14. Amalawi ena ndi zitsiru ndithu chomwe mukumanyozela kwanu kokongola kopanda nkhondo ndi chiyani, koma penapake sukulu ndi ya bwino i knw most of them sadapite ku sukulu ayi ana amagomo osadziwa ndi nkhuku yomwe mbava

  • Malwi remain the poorest country in the world aliyense amaziwa kale zimenezo nde ife tisiyen tili ku jons kuno ma passport tinapanga tokha transport nde #tjoo enanu tikudziwa ndikulila ndi mtima kuti simuzaonako bas but sorry ndinthawi ndipo zoti kuli zokhoma ai ndithu musamavutike timathamanazo tokha ngati zikukuenderan #satanic zanu mwayamba kumalawizo ndizanu koma palibe kupangira mwina we’r still here in jons ngat kubanja kwa2 kumaoneka kusitha haa nde munthu wake ndineyo ndithu ndilama zakenso szakumalawi kwanuko aa za jons mukunenayo enafe tikuimva bwino ndithu #mxxm #stupit

  • ZAZII. ALIYENSE NDI WAMKULU. AMASANKHA YEKHA WHERE TO STAY AND WHAT TO DO. WHO ARE YOU TO JUDGE. ANTHU AYAMBA LERO KUYENDA? MIGRATION WAS THERE, IS THERE AND WILL BE THERE. PAMENE WINA AKUONA BHO WINA AMAONERA MWINA YOU CAN’T ASSUME SOMEONE IS CRAZY COZ THEY WANT TO TRY SOMEWHERE ELSE. NDIYE UMBULIWO.SUKULU YANU SIMUNAPINDULE NAYO.

 15. Changa ndichisoni kwa omwe akunyoza dziko lawo. …kumalawi ndi kwabwino ukakonzekera koma ife amalawi ambiri tiri moyo oti tazipezelanji……..nkhuku zomwe zikunenedwazo ndi free range tu pamalawi. …..ufulu tikunyadira kunowu dziwani kuti eni ake anauvutikira……..tiyeni kumalawi tikamenyele nkhondo dziko lathu ….nthawi ndiomweyi yokadzegula ma ptc

 16. Der is no such thing lyk Malawians are suffering in or near Lindela,Get facts first n den wena stupid cying ukuth u r going to beat foreigners up uyi silima ndoda Nelson Mandela must b turning in his grave

 17. Amanga kuphela Akulanto eyokuthi abantu baseMalawi bayahluphekha elindela mina ngihlala maduzana kulendabo.Masizwane bafethu, ma ukuthi alisela ndaba eyokubala emaphepheni kungcono lihlale emakhaya cz wat u the so-called news24 Malawi are updating Abig SHIT!!!!

 18. Home is best, even Kamuzu came back after a long time. Mipaliro ndi zibonga zama Zulu ikazayambiranso, muzalalaka kubwera kumudzi kwanu, Malawi mudzamuona ndi maso koma simudzamfikira. Musaganize kuti ma bus boma limkatumiza aja azabweranso kuzakutengani nthawi imeneyo idatha nayenso tili pa mabvuto. Rand nayonso ikungogwa ndiye musatinyoze ndife abale anu. Palibe amalandira R5000.pamwezi kumeneko. Ntchentche inati mmbuyo mwabwino mtsogolo mwabwino.

 19. Chikumbutso zidana naneso ndinali phunzitsi kumalawiko ndikudziwa zakuwawa chifukwa ndiwe Aphunzitsi pano ukulandila zingati?dilu yamabuku ilipo nanga choko kkkkk?

 20. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

 21. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

 22. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

 23. Zoona munthu ukayisiye Volosi Chicken Beef cocacola 2 litre Castle lagaer Heineken Hansa Amstel Amarula Jack Daniels mabeybie okongola makaladi kkkkk nkupita dziko laumphawwi tiziti mutu wako ukugwira bobo?

 24. Dnt take advantage to talk nosense..enanu mukuthawa ngongole, ena mudasya mimba kuno..what ever the case, malawi is ua root.akayamba kkumenyani dnt seek help from our government..ife tkuphunzira momuno,,kudya ndkupeza ndalama momuno en we’re still survive..

 25. Simukumachedwa kupsya tonse tinjinga kugulitsa,tima dvd,tima screen ashame of u don’t forget that u Malawians OK,muzatipeza kwanu mkwanu mthengo mudalaka njoka

 26. Amalawinso Apa Alemba Kuti Muli Desperate Ku Joni!Komanso Mukunyoza Amzanu Kuno Mukupindula Chani?Akatero Ayambe Kukudulani Makosi Zeno!

 27. Always loosers give up,u gave up for ur country but wen ur chased with xeno u wanted our taxes to offer u buses to come home we only did that out of love but be ashamed of urself,anzanu kumalawi konkuno tikumwera 30 thousand aday inu kumalephera kuipeza kumeneko hence forth ati alikujoni shame!! Osangobwerako bwa muzizadulansokho mulemeletse dzikolanu.am jst sick of u guys

  • Hey man musalankhule mokuthamau cozy enafe timachoka mafamily ovtika mot KT a2 adye akudalila ife ndye musamalankhule ngat a2;otse Atari abwere kumeneko mungawapatse zochita ine2 ndinali komweko last DEC a2,akvtika kumeneko iwe omwera30 osawathandiza bwanj mind ur mounth broy

  • ZAZII. ALIYENSE NDI WAMKULU. AMASANKHA YEKHA WHERE TO STAY AND WHAT TO DO. WHO ARE YOU TO JUDGE. ANTHU AYAMBA LERO KUYENDA? MIGRATION WAS THERE, IS THERE AND WILL BE THERE. PAMENE WINA AKUONA BHO WINA AMAONERA MWINA YOU CAN’T ASSUME SOMEONE IS CRAZY COZ THEY WANT TO TRY SOMEWHERE ELSE. NDIYE UMBULIWO.

 28. Guys tisamaname munthu amene amalandira K200000 kumalawi ndi graduate pamene ife timaipanga pa week zikungofunika dongosolo basi lamapepela otherwise me am here to stay

 29. Those of you who have not been to South Africa can be cheated.They sleep in tin houses chigulu which house are you referring to? The type of work is tennantship or another slavish work

 30. He he he Joni ndi imodzi koma kusiyana ma film…enafe konkuno timayendera njale za nyatwa, nyumba za bho, ndalama sinkhani komanso a police kapena a home affairs ndi amzathu ndipo sitimawanyumwa popeza mapepala okhalila kuno tili nawo.
  Zimangofunika ndondomeko zinthuzi abale.

 31. Mukhale ku South Africa konko musabwere kuno ku Nyasaland ayi mabvuto ali kuno timawakwanisa tokha inu simungamake DZIKO lonseli mwini wake ndi MULUNGU.

 32. being in S.A for 10 years now and this is my home as well. they can deport me but I will come back again. kwathu kunalowa mbola besides when u doing better mmm too much jealous.

 33. Ndikatan ku malawi nkhuku nkudya dairy no matter what never go back to malawi koma na ine ndi akubanja anga tagwirizana zokhala kujonz kaya tiliman chöncho mukalamba nsangamuona

 34. Zoonadi ena ambili atulutsidwa,masiku 4 apitawa,mmodzi mwa azibale anga awiri omwe anagwidwa 4months ago wabwerera kunyumba kwanga,zili bwino ndithu,sitibwera ku mpanjeko unless mutapha wamathanyulayo kaye,finish.

 35. kwathundikwathu tazabwelela nthawi ikwana osati pano aliyense akufuna kuchitabwino palibe mnthu angavomele kuti azikhala ovutika padziko lapasi ndyeno nafeso tikuyesesa pamphavu zathu chifukwa chonenepesa hkhumba cchiziwikatu kusiya ndikungokha pakhomo akutitu kobwela kokha kamalaula sichoncho ndiposo akuti pofela salambula

 36. Home is best ever,,,i am also here in SA Midrand Joburg, but even rand by now is drown heavy and food rent are are very expensive. If you can count down all that,, you better make business home or work and get paid mk50 000 but you stay at your home. 85percent malawian are getting that peanut. Lets not to our fellow malawians. They will not welcom us after we go home with nothing. Luck me i did what i came here for and increase wth others. But i still do not have money. South africa is good to those who know hand works. Chilungamo sichiposa apa,,amalawi ambiri amagona mu mikhukhu yoti ngati mmagona nkhuku kamba kosakwanisa ma kulipila room. Room ya one bed ndi r700 above=mk30.000. Food r450=mk19,000. Nde umalandila mk100,000 ukhala nd zingati? Uchoseso transport. Tiyeni tizinene zoona kuti, bola poti pamwezi timapezako kusiyana ndi kwathu.

 37. Once again,akuluakulu ku SA chonde kuno zibwenzi zanu zikuvuta kumatipempha ndalama daily chondechonde mukalandila ma randwo muzitumiza pena tikumachita manyazi mkumangowathawa take knot that pliz

 38. President Peter Muthalika ndi boma lake wakhazikisa kale thumba la ndalama kuti athandize mzika zomwe zili ku #LINDELA.president Peter wanena kuti kuli bwino athandize mzika zimene zikuvutika ku south africa kusiyana ndikuti ndalama agule chimanga kuti anthu athandizike.komanso mene ndikuwonela amene ali ku Lindela akupeza mtendele wa dzawoneni kusiyana ndimunthu ali ku mpanje amene akugwila job daily.ku Lindela tea ndiwamkaka.pogona pabwino.kulibwino ndikhale ku Lindela kusiyana ndikupita ku mpanje

 39. We r all human beings take care of urselves en Malawi is ur Country basi even u stay longer but u r a Malawia,a good example Bushil

 40. Sindingabwere ine kumeneko ndidzidzalandira K40 000.00. Pamwezi ndalama yoti ndimalandira after 7 days. …..never adzachoke kaye bwampini ndidzabwera otherwise life is good here timadya bwino, kuvala bwino everything is affordable

 41. God is power,, its nt gud to go back home while u r nt well prepared coz Malawi nw is full with hard problem z,,,ndalema navo mweee,njala too much

 42. Any country there’s deportation! Y b surprised? 2 b @ Lindela doesn’t mean u r a stupid, but u hv no proper permits documents! I hv bn 3 tyms @ Lindela but still now am in S A! Shame 2 stay the so called Malawi!!

  • God blessed any country on earth n God loves anyone N God gave us brain to guide us to know what we can to improve our lives! There’s enough minerals in MW that can develop the country! The problem is ppo hu calls themselves leaders r not qualified 4 that job! They r qualified only for stealing Gvnt money but not to develop that poorest country! We only need gud leaders thats all

  • God blessed any country on earth n God loves anyone N God gave us brain to guide us to know what we can to improve our lives! There’s enough minerals in MW that can develop the country! The problem is ppo hu calls themselves leaders r not qualified 4 that job! They r qualified only for stealing Gvnt money but not to develop that poorest country! We only need gud leaders thats all

 43. When ur staying in Mzansi u must have a friend or a close relative so u can’t be desperate when ur released perhaps these guys had their lodgings where they dwell wìth friends or family members before they were netted,obviously in circumstances like this they’ll go back to their folks.Don’t tell us lies.Just tell us that Rsa gvt release illìgal foriegners from repatriation camp,thats all. No foriegn man dwells in the street or under bridges

 44. Timaoneka ngati opusa akagwira amakusiitsa katundu nthawi zina ndalama zako ku mabank komanso mwina kwamzungu zoti wagwira mwezi onse salary sadakupatse mzungu thats why ndianthu odyelera amenewo

 45. zateremu apitilizabe kutigwirako?hahaha ndidyeno Volosi ndi Iwisa mtima uli mmalo kakakaka Ng’iyaithanda londoleyo.

 46. I will never go back to malawi though home is gud whats the use of being educated and receive peanuts southafrica is anice country its amatter of getting the right documents before ucome life is gud here guys

 47. i think we must go back home amene tikusaukisa ziko lamalawi ndiife tili moyenda chifukwa nzeru zilo mwaife amene tikumachoka mmalawipo lupita kwina

  • Ukunama iwe ine bwanj ndmavaya kenya n south Africa bwanj xkuyenda ku malawiko chmene ungadziwe amadalitsa nd mulungu mu njira xosiyana pali ena ku malawiko anangobadwa kumudz osapitako even mtown koma mulungu anadalitsa nd chuma

  • zoona braz nanga halfvya amalawi ili moyenda ndichilungamo chimenecho anthu oti alamule ziko lija amalephera kusankhidwa kamba kaife tili moyenda fe.mavoti athu akufunika kwambiru

 48. vyako ivo,kweni picture iyo nja population iyo yikawa kulindela nyengo iyo,Coz this picture is old hope u get from google,uleke utesi admin nizakubafula uheni chomene

 49. Kkkkkkkkk jozi its where we belong for now. Not for ourselves but to make our malawi better as well. We only need chance to get wat we want then we will silently go back to our malawi

 50. Kkkkkkkkk jozi its where we belong for now. Not for ourselves but to make our malawi better as well. We only need chance to get wat we want then we will silently go back to our malawi

 51. Useless people I gather a certain person is arranging to go back who was transported by Malawi Government back here.Never bring them back again they are the lazy group and nomadic leave them to find their own way out

 52. Useless people I gather a certain person is arranging to go back who was transported by Malawi Government back here.Never bring them back again they are the lazy group and nomadic leave them to find their own way out

 53. Life is gumbo as we gumbling here until Malawi adzakhaleso wabwono ngati mmene analili kale mukadzachotsa that gay President we r coming,kuti gwila lero mawa kubweleranso

 54. Life is gumbo as we gumbling here until Malawi adzakhaleso wabwono ngati mmene analili kale mukadzachotsa that gay President we r coming,kuti gwila lero mawa kubweleranso

 55. Bodzatu ili panopa ticket ukumadula wekha yobwelera kumudzi apo bii amangokusunga konko koma zowatulutsa anthu kulindera ndiye sizoona amwene mwanama eish

 56. Bodzatu ili panopa ticket ukumadula wekha yobwelera kumudzi apo bii amangokusunga konko koma zowatulutsa anthu kulindera ndiye sizoona amwene mwanama eish

 57. This matter should not involve government because these are people who do not have guts as they preferred to stay in the Rainbow nation when their colleagues were being repatriated back to Malawi. Mukhale konko after all we have a lot of financial problems here.

%d bloggers like this: