Khonsolo ya mzinda wa Zomba yalimbikitsa anthu kuchita masewero olimbitsa thupi
Khonsolo ya mzinda wa Zomba yalimbikitsa anthu okhala mu mzindawu kuti adzichita masewero olimbitsa thupi popeza amathandiza kuti thupi lidzikhala la mphamvu komanso losadwaladwala. Wofalitsa nkhani ku Khonsolo ya mzindawu Sylvia Thawani ndiyemwe wayankhula izi… ...