Amangidwa kamba konyoza President pa Facebook
Anthu awiri amene amatsogolera anzawo pochitila mtudzu President ndi kumema anthu kuti achite zionetselo anjatwa. Izi zachitika mu dziko la Tanzania limene Mtsogoleri wawo John Magufuli wayamba kuonetsa makhalidwe achilendo ofuna kupondeleza ufulu wa anthu.… ...