Neba za ligi sakupanga nawo: Bullets 0 KB 0
Maule, yang'anani kumbali. Chaka chino timu yanu za ligi sikupanga nawo. Kapena mwina tingoti kwa iwo sinayambe. Khalani kumadikila raundi yachiwiri, paja timu yanu ndi kumadzulo. Chifukwa zimene zawachitikiranso lero ku Lilongwe, mavuto aja akupitilirabe. … ...