
Bambo wadzikhwezera mkachisi
Bambo wa zaka 45 m’boma la Thyolo wadzipha podzimangilira mkachisi kamba koti nkazi wake anapeleka ku kachisiko ndalama yose yomwe anapeza atagwira ganyu. Nkhaniyi watsimikiza ndi mneneli wapolisi ya Masambanjati m’bomali, a George Kaleso, omwe… ...