Imitsani kaye Airtel Top 8 yonse, apo bii tikatenga chiletso – yanyangala Wanderers
Timu ya Mighty Mukuru Wanderers yauza bungwe la Football Association of Malawi kuti liyimitse kaye masewero onse a mpikisano wa Airtel Top 8 pofuna kudikira chigamulo pa apilu yomwe ikufuna ipange ndipo yati apo bii,… ...