Chilima akakhala nawo pa mkumano wa ophunzira a Chikatolika ku Sukulu ya Ukachenjede ya Malawi
Wachiwiri kwa mtsogoleri wadziko lino, Dr Saulosi Klaus Chilima, akuyembekezeka kudzakhala nawo pa mkumano omwe wakonzedwa ndi ophunzira a Bungwe la Katorika ku Sukulu ya Ukachenjede ya Malawi ku Zomba pa 4 May chaka chino… ...