Asilamu atentha dambwe ku Kasungu
Asilamuwo atentha dambwe m'mudzi wa Mchinga kwa mfumu Njombwa ku Kasungu chifukwa gule wamkulu anagwira mwana wa mtsogoleri wachisilamu kukalowa naye ku dambweko. Malingana ndi wailesi ya Zodiak, gule wamkulu anagwira mwana wa mtsogoleri wachisilamu… ...