Nayonso Premier Bet yazituluka – ati chuma sichikuyenda, ma agent ntchito yatha basi
Kapena mwina a Malawi tasukutsula mmaso pa njuga mpaka takhaulitsa mzungu? Koma a kampani ya Premier Bet ati vuto ndi chuma. Ndipo tsopano ayamba kutuluka msika wa ku Malawi. Awo paulendo kutsatira DSTV. Kampani yotchuka… ...