Msonda azitaya, atuluka PP
Chipani chija chikutha anthu akuona. Mneneri wachipani chostutsa cha Peoples’ amene anakakamila ngalawaya chipanichi ngakhale mtsogoleri wake atachithawa, a Ken Msonda, alengeza kuti basi iwo alekana nacho chipanichi. A Msonda analengezaizi pa tsambalawo la pa… ...