Wapolisi waombera chibwezi naye nkuziphanso
Pawiri pawiri sipauzilika: apolisi ati wapolisi nzawo yemwe wapha bwezi lake m’mawa wa Lachitatu kenaka naye ndikudziphaso, anali pa banja ndi nkazi wina yemwe anabelekerana naye ana awiri. Wanena izi ndi ofalitsa nkhani za a… ...