Tikhala tikutsimikiza unzika nthawi ya kalembera wa chisakho – NRB
Bungwe la National Registration Bureau (NRB) lanena kuti likhala likutsimikiza unzika, pa nthawi imene bungwe loyendetsa chisankho la Malawi Electoral Commission (MEC) likuchita kalembera wa chisankho ndi cholinga choti a Malawi onse apeze mwayi olembetsa… ...