Samala ndi mlomo wako, muno simotukwanila Pulezidenti – sipika auza Chakwera
Mtsogoleri otsutsa mu nyumba ya malamulo a Lazarus Chakwera dzulo adzudzulidwa ndi Sipika wa nyumba ya malamulo. A Chakwera adzudzulidwa kamba konyoza Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika kuti iwo ndi kalonga wa mbava… ...