Samala ndi mlomo wako, muno simotukwanila Pulezidenti – sipika auza Chakwera

361

Mtsogoleri otsutsa mu nyumba ya malamulo a Lazarus Chakwera dzulo adzudzulidwa ndi Sipika wa nyumba ya malamulo.

A Chakwera adzudzulidwa kamba konyoza Mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika kuti iwo ndi kalonga wa mbava ndinso olephela ndi ogunata.

Richard Msowoya

Msowoya: Wadzudzula a Chakwera.

A Chakwera adanena izi lolemba pamene amayankhula mu nyumba ya malamulo. Iwo adali kuyankhapo pa zimene a Mutharika adanena potsegulila nyumbayi.

Mu kuyankha kwawo, a Chakwera adakwelela Paphiri a Mutharika ndi kuwathila nkhoko.

“A Mutharika dziko likuwavuta, iwo ndi olephela ndinso ogunata,” anatelo a Chakwera.

Iwo adanenanso: “a Mutharika ndi kalonga wa mbava amene akutsogolera uchigawenga mu dziko muno, kulibela dziko la Malawi mwa psipsiti.”

Atanena izi a Chakwera, nduna ya achinyamata ndi masewelo a Henry Mussa anaima ndi kupempha a Sipika kuti adzudzule a Chakwera kamba konyoza Mtsogoleri wa dziko.

Sipika adanena kuti afufuze bwino pa nkhaniyo ndipo azapeleka chigamulo.

 Popeleka chigamulo chake lachisanu, Sipika adanena kuti a Chakwera adalakwitsa ndithu poyankhula udyo za Mtsogoleri wa dziko.

Share.

361 Comments

 1. Malawian tasithani munthu akulamulirayu ngwakuba kuno sanakhaleko anali garden boy kwa America atangomva kuti ndalama zaphweka kumalawi anakasiya ma green book

 2. Ndi mmene zikundipwetekela ine kumuona Peter alipa mpando, bas wina akumuikla kumbuyo, kusaganiza bwino! There are so many things need to be changed! Tioneko zina awa aPitala zawavuta! I think people who are supporting him wakudyesa chibanz!

 3. PALIBE muthu angakhale mmodzi amene amafuna kuuzidwa chilungamo pazimene akuvhita amalawi tinazolowela kuvomeleza kuti zithu zili bwino pame ne pansi pantima tikunva kuwawa thawi zonse chilungamo chimawawa NDIPO muthu wachilungamo athu samukonda

 4. Nyumba Yamalamulo Yaulendo Uno Yagwira Ntchito Bwino Chifukwa Cha Dr Chakwera Ndiena Otsutsa Izi Zimathandiza Olamula Kuchangamuka Pakuchita Zithu.In Malawi We Nid Pple Of Chakwera’s Type.My Vot IS Yours

 5. Kod Inu Mafuna Kut Achakwela Anene Kut Zinthu Zikuyenda Bwino Pamene Zinthu Sizilibwino? Chilungamo Chmawawa Zomwe Anend Achakwela Ndizowona Uyu Pitala Ndimunthu Osayidziwa Ntchito Yake Ndipo Ndimunthu Okanika Zot Dziko Muno Tili Ndi Tsogoleli Zodziwa Yekha Iye Pitala

 6. There is a big gap between the state President and the party President, so Chakwera should be careful indeed, who told him that to be in opposition means insulting the? Kumakhala ndi umunthu abale.

 7. Pano Peter akuti Chakwela ndi wamisala inu mwaombela manja. Chakwela akanena kuti Peter ndiwa bodza lnu mukuti Achakwela atukwana pulezidenti. Olakwa ndani?

 8. Bola chakwera akulimbana ndi munthu mmodzi koma pitalayu akulimbana ndamalawi 18million … Pitala akutizunza magetsi tinayambira kudandaula muja kuti akuzimitsa mwachimidzi , wati bhowa bwanji iya!!!!

 9. APITTER PAN0PA SITIKUWAFUSA ATIZUZA M0KWANILA , MBEU TIKUMAZISUNGA NGATI MKWANDA WA, MCHIUN0 KUS0WA K0GULITSA B0LAS0 AKADALAMULAS0 KUTI TIZIKATCHA MALIWA KUTI TIZIPHA MBEWA Z0CHULUKA KUTI TIGULILEK0 FERTILIZER. TI0NEK0 KUSINTHA MU 2019.

 10. Chakwera ayiwala kuti anasankidwa ndi anthu kuti alowe mnyumba ya malamulo,amayankula ngati akulota mbuzi yeniyeni ine NDE sangandinamize

 11. koma Chakwera siolakwa he is speaking on the behalf of malawians.wat he is speaking is wat everyone knows.amene sakudxiwa kut opitala ndiokuba ndan.ndan sakudziwa kut walephera kulamula.koma anthu akudana ndi chilungamo.Bravo Chakwe umakwana ase

 12. In Malawi any leader who is a thief is a good leader… From grassroot we dont call amfumu as mbava but gogo…Kwenikweni a president ndiye eee a visionally leader

 13. Hon Mr Chakwera bolatu mubwelere ntchito yanu yakale ija ya Ubusa zisiyeni zinthu za dzikoli yambaninso kudyetsa nkhosa za Mulungu.zinthu za dzikoli zikuchedwetsani.

 14. Chakwera is the only politian who wants Malawi wa bwino not mmene ziliri panomu. Ogwira ntchito mboma saonetsa mbali koma their said imaoneka when voting. Musanyengedwe ndi fundo zomwe a DPP akunena kuti your salaries shall be increased. Why increasing things that shall not be given in time?? Dr. Chakwera 2019 bomaaaaa!!!!!! Winawe ulirira keep on using these undemocratic medias kkkkkk

 15. Abusawa ali ndi mantha komanso sakugona tulo.Tsono ngati mukumatukwana chonchi muli kunja kuli bwanji mukazalowa m,boma.Kale ndinkaganiza kuti kutukwanizana ndikwa anthu osaphunzira koma ayi anthu ophunziranso ndi mbuli zenzeni.

 16. In other way Chakwera is Yona so we need to Sink him in Indian Ocean thereafter we shall come up with aprove whether he’s indeed man of God when he getts swallowed by huge fish and spitted to where God chosen him to preach His news

 17. Kma ngt mkuluyi amkangodya chakhumi cha akhristu ndkukanika kusogolera mpingo ndiye mwati akufuna azasogolere Malawi yenseyi zizatheka? Osamangolongolora cfk uli pa bench ayi usayese kulamulira dziko ndizophweka Yona

 18. pali anthu ena omwa amafuna kuti dziko liwatame ndikulankhula,, pomwe kulankhulako kumakhala kosathandiza, kumangozitukwanisa ndi kunyozedwa.kulimbana ndi president mmalo momakamba mfundo zothandiza,

 19. Nkhani ndiyakuti chilungamo chimapweteka.basi! tangoganizani kuno ku Zomba magetsi anazima dzulo 8 Oclock mpaka pano sanayake ndiye ndikumafusa kuti mzipatalamu zinthu zikukhala bwanji?

 20. Zasimikizika sopano kut a chakwera akufuna kuchosa a msowoya u vice president at kamba kokwiya ndi kuchose dwa kwa speech yawo mu Hansard ,izi ndi chisimikizo kut mia nda mmene aku mufuna a chakwera kut asakhale runing mate pa zisankho zi kubwera zi!

 21. Chakwera simply called a spade by its name. Nothing wrong. Akuti chuma chikuyenda bwino, nanga bwanji zinthu zikukwera mitengo. Kunamizidwa yayi lero.

 22. man of God ochakwela thawi ino ndiyokhoza zolakwika za olamula kuti mwina tizakuvoteleni ositi kunyozana.Ife achinyamata tikufana pulesidenti opanga chitukuko cholozeka,ndikukhimitsa lamuloro lolemekeza anthu ogwira tchito zosiyasiyana powalipira moyenelera osatikuba

 23. man of God ochakwela thawi ino ndiyokhoza zolakwika za olamula kuti mwina tizakuvoteleni ositi kunyozana.Ife achinyamata tikufana pulesidenti opanga chitukuko cholozeka,ndikukhimitsa lamuloro lolemekeza anthu ogwira tchito zosiyasiyana powalipira moyenelera osatikuba

 24. Chiyambi cha mavuto onsewa ndi malemu kamuzu coz ndiyemwe adathamangitsa azungu mwachangu ndikubweretsa ndalama yoti kwacha mkuchotsa ma pounds now iye mavuto anathana nao coz anafa

 25. Kkkkkk chakwera ngati wathawa zamulungu kuthawira kundale ndiye mungayembekezele zinthu zabwino mwa iye?
  Chifukwa munthu amene analandira yesu muchoonadi sangayambe ndale
  Ndiye kuti maganizo make Ali pa chuma osati chipulumutso
  Papeto make ndikutukwanako
  Angopotoza amalawi mmalo mopeleka zitsanzo zabwino
  Mulungu anamukwiyira sangawine ameneyo walemba mmadzi

 26. Munthu kumuthawa mulungu ndi muganiza akazalamulira dziko azatha kuuza anthu zabwino, mulungu adawatuma kuulalikira mtundu wanthu, sazalola nyasi izi.

 27. He who knows that he knows not is an intelligent but he who knows not that he knows not is afool just leave him,Dr chakwera should continue shouting on tragedy we malawians suffering who can rebuke the president among you its only chakwera can, mcp 2019

 28. Vuto ndiloti anthu amasangalala ndikuti president ndi nduna zake azinyoza CHAKWELA pomwe akati mawu omwewo akuyakheni mumati ndionyoza ndiye azimuopa poti iye ndi president iyeyo alekenso kunyoza tsogoleri wa maso mphenya osati obela ai MCP MOTO KUTI BUUU KUOTCHA CHIMANGA

 29. Ochakwera oli ndi phuma kwambiri mpofunika osamathamange mwazi chifukwa songawine chinsankho ndi phuma limeneli zotsatira zake odzadyara bp okadzagwapasi koma odzitenga ngati kuti iwowo owina kale koma odikire omenewa kkkkkkk

 30. Chakwera Wapakamwa Ngati Pa Dzenje Lambewa!Chakwera Akufuna Kupusitsa Ngati Munthu Wabwino Ndale Zonyozana Zinapita Ndi Bakili Muluzi.

 31. Ngakhale Bible limanena momveka bwino kut tiyenera kulemekeza atsogoleri athu.Aliyense ali ndi ufulu olemekedwa posatengera kochokera,mtundu,maonekedwe ndi zina zotero.

 32. Truth is painful its better chakwera is talking the truth than anyone in the Parliament while President Piter muntharika is bzy liying the people of Malawi nw ur bzy hating chakwera bcz he tell the President truth Mr speaker ur so stupt plus muntharika is also stupt futsek.

 33. Kodi kutukwana mumakuziwa inu?. Chakwera anena kuti pitala ndi kalonga wakuba pali kutukwana apa. Inde ndizowo muthalika ndichibamva chachikulu ndipo chowononga miyoyo ya Malawi.

 34. Zikukomera mbuzi kugunda galu,koma galu kuluma mbuzi walakwa,a prezdent omwewo adamunena Chakwera kuti ndi wosaphunzira,nde lero Chakwera wabwezera pogemula kuti APM ndi Kalonga wa Mbava,walakwitsa?Muziona zodzudzula,panthawiyotu APM mudamuombera mmanja.

 35. munthu akathawa pa maso pa mulungu amalowelera kwambiri kuposa amkhalakale pa machimo ngakhale bwato limayamba kumila. ku ndale kulibe uzimu munthu amadalitsika akatembenuka mtima osati akayamba kulalata. ndale ndi ndale ndipo kulibe ndale za uzimu.

 36. Chomwe ndimadziwa nchakuti yense adazemba utumiki nkumachita zina mutu wake sumagwira,and this is exactly what Chakwera is proving. Shame on Chakwera that he has even forgotten himself,where he is,why he is there,how he got there.Chakwera is bringing disgrace to MCP,and if Chakwera continues to provoke Malawians by insulting our beloved leader,MCP will miserably because the more he make un necessary noise,the more he distance himself from presidency.I wish I were in John Tembo days, but with Chakwera at the helm of MCP,I dont see any nearness of MCP forming government

 37. Ndale Za chimidzi Mr Chakwera, you must learn how to respect the Authorities!! I now understand that you went to a Bible School and you better go back to your profession because mu ndale Anthu odwala mutu waching’alang’ala sakufunika!!

 38. Mau aketu sanali akulu koma anali owawa chabe Prince of Thiefs basi nanga o Chakwera anaonjezeraso ena mauwa ngat kkkkkkkk moto uwo kuti buuuuu kuyatsiratu nsalu ya makaka a chimanga kkkkk

 39. Kapena tiganize kuti che Chakwela liwu loti opposition leader sakuligwirisa bwino ntchito? Kuyambila 2014 mpaka lerolino kususa kwake kunyoza basi no time for developments or campaign

 40. Main parts 4 the person to be a president, (1) Well Educated,(2)Critical thinking,(3)A very good visionally leader to his/her country,(4)Respecting other people’s view osati kunyoza ndanena zonyoza apa? If it could be that chakwera wants to help Malawi he should not behave like that! but together they were suppose to solve the problems,Mr chakwera to be president its not joke and to lead the Malawians its not easy! it need an experience! Lastly chakwera stop talking your stupit points in that house its 4 Malawian!

  • Nde a Malawi anayamika? ukuwona ngati Dpp sikupanga zina zabwino ikupanga koma munthu sangapange zokondweretsa a Malawi tonse pamodzi ayi pomwe akukoza kwina kwinaso kumakhala kukuwonongeka ndani angakwanitse zofuna za Malawi mu zaka 5 zokha? Can’t you differeciate 30years with 5years? ngati ulindi mzeru Kamuzu ungayerekezere chakwera? Am not hating mcp but am hate chakwera with his stupit negative report vuto lako ncha? ngati ukufuna uyambe wamuphuzitsa kuti kodi kutsutsa amatani wosati za mwano, nsanje, kufuna kusokoneza zokambilana ngati mu mnyumba ya malamulo alimo yekha kumeko nde kuja pa chizungu timati kugodomala/kupepera.

  • leadership sikuphuzila koma mphaso yochokera kwanamalenga ,kodi peter mesa ndiophuzira nanga zikuvutila pati?ngati inu ndiawo mukudya bwino sionse mukuenera kufufuza bwino zithu sizili bwino

  • Limenelo ndi bodza leni leni ndichifukwa chiani mwana akamakula amayenera kupita ku sukulu koma chosecho mukuti utsogoleri sulira ma phuziro nowdays even to be a good prophet or anyleadership you it need education as a key to success, even Jesus was busy to teaching his disples 4 them to be knowledge of how lead other people there4 tisanyoze sukulu yomwe ena amayilirayi ayi! munthu ngati sanaphunzire mokwanira atsogolera bwanji anthu kodi akhungu wokhawokha angalondererane njira? And thats why he always leading people to have demostration chifukwa sakudziwa ubwino ndi kuipa kwake kwa chinthucho ndiye limenero ndi bodza sukulu its a key!

 41. Amalawi ukape anazolowela kudya chogwada atulele uyu akakula mutu ngat Bingu sterdium amat alamula dzko? akwele chakela tione zina hahaha!! tauzani siufumu uwu.

 42. Ndale zotukwanizana sizingasithe kanth.Achakwera ngt busa kmso ngt mtsogoleri sakumayera kmalankhula motere.asamayiwale kt kumene kwasala tchile ndikmwe moto ukpita.Achakwera mwawonjeza!!!!!!!!!!!!!

 43. CHAKWELA SANGAWINE PA CHISANKHO 2019, NDICHIFUKWA WAYAMBILATU KUTUKWANA ALIBE MFUNDO. ANABAIBA NDALAMA ZA CHOPELEKA KUMPINGO KUTHAMANGILA NDALE ALI NDIKABE ZAMBILI WAGWANAYO. PALI MAU AMATI SIUTCHULA UFITI USAKUUDZIWA AI. UKATCHULA UFITI NDIYE KUTI NAWE UMAULUKA.

 44. Admin please! Try to avoid this stupidness; Iam sure you have the right to sit down and think before you write and post trush like this one. Otherwise we like this page.

  • Adm Wa group lino nayeso ngoperewedwa mzeru coz amafuna azitukwanitsa azitsogoleri nkhani zake. Ine I love Peter , chakwera , even atsogoleri azipani zonse koma amatipangitsa kuti tiziyambana nao ndi a Malawi 24

  • Nkhaniyi ma page ena ayika dzulo phuzirani kuvomeleza pakalakwika ndie kuti anthu ayikhulupirira mcp ngati mukuonesa kusavomeleza muli ku opposition kuli bwanji mcp ilamulire? ndambiri tikufuna kuti mcp izapambane koma sibwino kusapota kunyoza ndie chakwera ndi dausi zisiyana pati pakuti tikufuna kuti zinthu zisinthe.

  • koditu pakati pa anthu olakwa okhaokha sipapezeka okhoza koma wina apange zolondola komaso muvetsetse ku parliament sapangirako campaign zonyozazo akapangire outside parliament pa msonkhano wa ndale make a difference between arguments and non-arguments.

  • If you say thieves get angrier when told they are so,what do you mean?Are you licenced to detect and establish someone as a thief? I mean who made you the DPP watchdog?The utterations you and your cronies make reveals your total ignorance and stuipidity which words cant express.You are degrading yourself whenever you insult the leader and you will never succeed,DPP will rule for decades to come y

 45. Kodi cakwela ndkanyama kanji kt evryday tizingova zayiyo kod OSUSA ALIPO YEKHA Munthu uyu amalawi cenjeran nayo akuoneka kut ndiosokoneza

  §§§ (anathawa utumiki wa Mulungu ndikuyamba za mzikolapans)

 46. Mvuto lakuti ngati uli munthu wapatsidwa Udindo mudziko la nyasalande olo adzichita zopusa anthu amafuna mudzimulemekezabe chifukwa Nkhani yayikulu sikuti achakwela adanyoza Kapena kutukwana muthalika ayi iwo adafotokoza mwatchutchutchu zowona zeni zeni zomwe akupanga pitala komaso kwa ine ndikuti achakwela apitilize pomwe adasiyila paja mwina zina zingasinthe

 47. chakwera differentiate the church and the pariament, u are not alone in the house there are also other pple in the house why u alone? We are enthusiastic to hearken about the points that will develop this country not ur nonsense Chakwera please. defiance to the president will never help the pple who sweated to put where u are. U r getting allowances daily but we prebians we dont c development. ALA KUKHUTA WHISKY dont go to parliament if u are drunk or mutasuta chamba. Umenyedwatu chatsika oh! chakwera

 48. #copied…”Samala ndi mlomo wako, muno simotukwanila Pulezidenti – sipika auza Chakwera”

  So your mean this is the Chewa translation of “incompetent”, insensitive and a “Prince of thieves”. Be serious guys.

 49. Ameneitu alowepodi tione kuti alisintha bwanj Lawi lamotoli poti amat “the proof of pudding is in the eating” asamangolalata Ali pa bench..zikomo kumpando!

 50. Hopefully iam not being partisan here but the president needs to lead by example by not inflaming the already precarious situation by resorting to name calling.Chakwera too must refrain from such careless wording .All of them need to lead by example.To us ,these war of words are catastrophic .Anthuwa amsmwera limodzi coffee.Tisawamvere.But they should learn to avoid inflametally speeches.Practice civilised politics..This isnt campain period where you speak to please the electorate .Mind your words ,what are you teaching the junile politicians.Politics is the art of running a government not a platform for utterung useless words.

 51. Ife aMcp sitili kusekeseka ndi nthano ngati izi ndikudziwa kuti you have trying to pull chakwela down but to vote him is our main key

  • Iweyo sindiwe Mulungu ndipo ukutaya nthawi ndikulingalira zimenezo, munthu wanzelu sangasangalare ndi kubedwa kwa ndalama zochuluka chonchija, sangakhale okondwa ndi mmene akuvutila magetsi, sangakhale okondwa ndikukwela mtengo kwa katundu, sangasangalare ndi kugwa kwa ndalama ya kwacha, kwa okhawo osalifunila zabwino dziko lino mukhoza kumamufunabe peter koma kwa ena amene akuona kuti zinthu sizilibwino tikadakonda kuti malawi alamulidwepo ndi munthu wina monga mmene ziliri ku Tanzania komaso ku zambia kuli atsogoleri amasomphenya osati kakaka munthu amene alibe kuthekela kuli konse pakutukula dziko lino

 52. Vuto la a Malawi kudana ndi chilungamo,…..when the president insult chakwera kuti he is uneducated you people clap hands for him….when chakwera calls him the prince of thieves everyone has issues with him…..malawi will never develop with this blind royalty

  • Akanamaonetsa chitsanzo chabwino ngati m’busa. Kutsutsa kokonza zinthu osatikumangonyoza, akupereka picture yachabe kwambiri. I don’t think he can be a good leader.

  • Osward tamvera kuno, apatu anakakhala kuti Chakwera amalankhula zinthu zanzeru. Mutu wankhaniyi sukanalembedwa kuti, samala ndimlomo wakowo muno simotukwanira President ayi. Kutukwana ndikosaletsedwa anthu kutukwana, koma kuli ndimalo ake osakhala kuPaliamenti. Umuuze Chakwera kuti, akafuna kutukwana apite akachitinse nsonkhano ndiye kumeneko alindi ufulu okamutukwana mnzakeyo. Uku ku Paliament dzikolonse limankhala likumvetsera, zokambirana zomwe anthu anapepha kwa amphungu awo kuti awachitire kudera kwawo. Anthu amawatuma amphungu awo, kuti mukatipephere kumeneko ife tikufuna Sukulu, nsewu, madzi abwino ndi chipatala ndiye malo moti amve zimenezo basi zimvetsera kutwana kwamunthu wankulu.

  • #Jafali ….i didn’t hear any obscene language in what he said, unless ngati kunena mzako kuti ndi mbaza ndikutukwana i will understand….. otherwise u pipo r just building a mountain on a mole hill

  • Ngati a president atukwanidwa siwoyamba iyeyu kutukwanidwa ndiye chilipo chapangisa kuti winayo atukwane ndipo sizinayambe lero ayi, ambirinso mumamutukwana muma face book momuno ndiye tiziti inu muli a ulemu kapena ozindikira tangosekani pakamwa panupo eniake amadziwana #Zandale izi

  • Ndiye umuuze speaker wanyumba yamalamulo kuti Chakwera sanatukwane, chifukwa iyeyo ndiamene ananena kuti samala mlomo wakowo muno simotukwanira ayi. Ndiponso iyeyo speaker-yo simwanatu woti, mungamunamize iyeyo akudziwa kuti mau awa sioyenera kulankhula muno komanso amadziwa kuti mau awa akulankhula zowona. Kodi iyeyu Chakwerayu asanapite ku Paliamenti, amalankhula ngati munthu wanzeru eeh magetsi kuzimazima, eeh anthu akuba bwanji lero osapereka mfundo zimene zija kuti tione nzeru zakezo nzotani? Koma lero akuti, ndizikanyanyala zilibe phindu ngakhale utanyanyala anthu anazolowera ndim’mene mumapangira.

  • Adha ndinu abodza, ifeso chizungu timamva…..zimene ananena interpretation yake simeneyi pa chichewa. By the way, did u listen to Chakwera’s speech or perhaps read it……coz if u did u will understand that the speech contained more than what these pages r reporting. You also need to understand that whatever he said there did not contravene any laws of Malawi, even amene amkanenawo akudziwa

  • Kaya bola ndakuuza ndikumva kwako chizunguko, kaya nayenso speaker-yu amaganiza chiyani ponena zimenezi ndiye kuti anayiwala kuti umamva chizungu?

  • APM sichina ayi koma nkhawa coz mtumiki wamulunguyu sakubwera moyesa muzigawo zonse zamuno mmalawi,even kwawo kwa APM akutengeratu mavoti.Mbali imodzi ya Dedza ndikumene akuonetsa ngati mavoti achipukuta misozi adazapezeka kwa APM.Ndani amakondwera ndi munthu amene akufuna kumukhwefula paudindo umene ali? sizachilendo izi kuno kumalawi,anthu akudana bcoz of kulimbirana maumfumu ammidzi wat more upulezdent??Ngati ndatukwana mundisake mundipeza.Musiyeni kaye Lazarous alire maliro abambo ake amene tikuika mmanda mawa pa 19th Nov,2017.

  • Amanyimanyi Inu Taxyan Muwone Magetsi Ndi Deal Dekhani Muone January Ndi February Ngat Muzakmbe Zaubwno Wamunthu Businex Iliynxe Imafuna Mgetsi Tapangn Chete Muone Mundiuzaa

  • Ndinadziwa ine kuti munthu kungosiya kutumikira Yehovah nkuyamba ndale, hmmmmmm🙃🙃🙃🤔🤔🤔

   Ngati Yesu amene adaletsa Petulo kuwedza nsomba kuti amutsate akagwire ntchito ya Mulungu, kulibwanji Politics yomwe language yake ma verb ndi ma Noun ndi:.. Half, Chitsiru, Opusa, Mbava, Odwala, ……

  • …imagine he exercised it during his dictatory party he’s leading..he would be history by now…he’s enjoying with what he failed to provide for decades…

  • No Shoaib Bwanali. You are now twisting issues. That time of MCP era was a One Party government where you and me were all for that party. Take it or leave it we were all there. Buying a membership card to solidify or cement membership. So we don’t want someone this time of democracy to oppress and threaten each while we are all eyes open. MCP did not fail but did its part so did UDF (my favourite party). If one abuses government funds let’s not put that under the carpet.

  • Yes my dear brother. I don’t condone unnecessary behaviour that pull the already poor nation down. Flashing government resources into the drain helps no one. Such being the case let those who have better description of people whose character is wasteful handle those adjectives that suit them. Be it a thief or crook regardless of who the person is or what position he holds in parliament or nation at large. Leaders whose myopic leadership draws Malawi to a mediocre image due to their failure to deliver. We need leaders chosen through merit not political party addiction. I am a diehard member of UDF but with what Chakwera said in parliament I would better vote for him for presidency while I remain a #Yellow_Nation addict.

 53. Zimene akupanga chakwela zosokoneza kwambili .ndikozendikoze izi mukulakwa nazo muwoneka munthu oipa ochakwela aaa zoona andale ndi amodzi

 54. anaba 90b pano akuyenjezelanso zafika pa 200b mukuganiza kuti omwe akuonawo azingoyang’ana kuyankhula basi iwo paja ankamusuzula jb kikiki lero kwa iwo ndimwano ngati ntsogoleri sakuzilemekeza how can others give respect to him dzana anati chakwela akuyenera ku meto hosp kikikii zokomela mbuzi kugunda galu ………..

 55. ndiokuba uyu waba zopeleka kuthawa kubwela ku ndale chenjelani ndi anthu oooneka matupi ngati ankhosa koma nkati mwawo ili mimbulu yolusa

  • Chakwera ndi mbavaso tafufuzanh kuchipani kwao akuwuzani zenizeni. Khalani ofufuza mudzadziwa zenizeni kuti chakwera naye ndi akatundu pakuba.

  • Munthu Wakhala Pa U Mp 3 Years Koma Wamanga Chi Massion Cha 90 Million Mukuganiza Kuti Ndalama Watenga Kuti!!! Nanga Atalowa M’boma Angabemo Ndalama Zingati???

  • Amalawi mvuto ndi chiyani? Dziko lidayamba kulamulidwa ndi azungu mudawathamangitsa mwati adali ankhaza, panabwela kamuzu mudamuthamangitsa mwati adali wakupha, bakili adabwela mudamunena kuti ndi wakatangale, bingu amatimphwanyila ufulu, joice banda cash gate. Lero pitala mwati sakuyendetsa bwino dziko. Gwelo lazosezi sicha ayi koma ndikusawuka kwadziko lathuli. Pando uwu waupulezidetiwu ndimpando onana padziko lose lapasi. Munthu akaukhalira sangalephele kuwubela. Chifukwa ndi mpando wachuma. Nde musataye nthawi ndikumangokangana zazi ayi amene ukumuganizila iweyo kuti akhale pampando umewu zizakhalaso chimodzimodzi.

  • Which church has he stolen the money? Name it and mention how much I can pay for him unlikevcashgate .maizegate .escomgate and 2014 election gates .
   Munazilowera atsogoleri opembeza mafano osadziwa Mulungu okuba okupha But time has come and now is the time that change has started working in the minds of malawiana

  • AdmaD Isaac, thats naked true my bru, problem ndi yoti Nyasa ndi yotukuka pa Ndale…Nonses, palibe mtsogoleri angafike pa 70% ubwn wake bcz, Ndale zatenga malo..everybody wants to be a President. Shame on you, perekani mpata Inconomic freedom ifike- mwina anthu mkumanva zina.

 56. Kodi mbava imafunikaso kuipasa ulemu. Munthu akakhala wakhumba dzina lake lachiwiri ndi mbava basi. Peter mutharika chifukwa choonelera anthu akuba chuma cha boma osachitapo kanthu nde kuti iyenso ndi mbava.

 57. Chakwera iyi ndinthawino yopereka nzeru ku Paliamenti, pamene boma likulephera ndikumaliuza kuti pakufunika kuchita izi kuti zinthu ziyambe kuyenda bwino. Anthu azakukonda kwambiri ngati, utamapereka maganizo ako ku nyumba ya malamulo. Kaya boma liwaderera, koma anthu akhala atadziwa kuti Chakwera analithandiza boma koma bomalo silinazigwiritse ntchito. Ndiye uzaona ulendo wina anthu akukuvotera, koma ukakhalira kunyanyala ndiye uwonanso wekha. Sikuti ukanthandiza boma nzeru zakozo, ndiye kuti anthu anena kuti walowa m’boma ayi sakuiwalonso koma tsiku lovota azakuvotera kwambiri.

 58. My good people hear my good news, i am an Agents sent by
  the Lord superior Grand master to bring as many of those who
  are interested in becoming a member of the great illuminati
  temple, Becoming a Member of the illuminati. your
  qualifications are, Only those who can provide service for
  themselves, like the Politicians, Musicians, Business Man/
  Woman, student workers, traders ETC, and you want to be
  rich, powerful and be famous in life.You can achieve your
  dreams by becoming a member of the illuminati, and also get
  instant amount of $8 million dollars with a free home
  anywhere you choose to live in the whole world, and a free
  triple visa to travel to any country in the world, and a ring of
  riches, power will be given to you immediately after your
  initiation, i do business, I own a Construction company, and i
  also own one of the Biggest Electronic Appliance shop, and
  my family now lives in USA, i was once like you, me & my wife
  were financially down to 1 square meal a day, what kind of life
  was that to live, I lived in poverty until i saw an opportunity to
  be a member of the GREAT TEMPLE OF illuminati
  BROTHERHOOD and i took my chances and i have been a
  member for close to 10 years now. The higher you go the
  richer you become, it makes your business grow faster than
  you can ever imagine, illuminati brings out the talent in you
  and make you famous, as you become a member of illuminati
  order you will receive $8,000,000 US DOLLARS instantly on
  your Bank Account, there are many more other benefits you
  can stand to gain, so if you are interested to be a member
  contact us now on +2349027505789 or whatsapp me or Email:illuminatiagency2@gmail.com

 59. mmalo mothandizana kutukura Malawi wathu. mwayamba mum an got how a nizam a pa zithu zopanda pake. tieni tiyangane kusogolo Malawi mxanga. osati kukokerana mmbuyo ixo ndi ndale zakare

%d bloggers like this: