Otsutsa ati anyanyala zokambilana ku nyumba ya malamulo

317

Pamene zokambilana za aphungu ku nyumba ya malamulo zangoyambapo, mtsogoleri wa zipani zotsutsa a Lazarus Chakwera anena kuti iwo ndi anzawo ayambapo kunyanyala zokambilanazo.

Malinga ndi a Chakwera amenenso ali mtsogoleri wa chipani chotsutsa cha Kongeresi, iwo ndi aphungu awo ati ayamba kunyanyala zokambilanazo ngati a boma sabweletsa mu nyumbayo nkhani yokhudza zisankho.

Lazarus Chakwera

Chakwera: A Mutharika ndi a bodza.

A Chakwera adaulula izi pamene amayankhapo pa zimene a Mutharika adakamba potsegulila nyumba ya malamulo lachisanu.

“Ndipo a Mutharika ndi abodza, anatilonjeza kuti abweletsa nkhani yokhudza malamuo a zisankho, koma mmalo mwake tikuona palibepo,” anatelo a Chakwera.

“Ndipo ife tikunena lero kuti ngati nkhani imeneyi siyibwela pano, ife tiyamba kunyanyala zokambilana mu nyumba ino,” a Chakwera anaopseza motelo.

Mwa zina, malamulo a tsopano ovotela akunena kuti munthu opambana chisankho cha President azikhala kuti wapeza mavoti opyolera theka la mavotiwo.

Zikuoneka ngati chipani cholamula cha DPP ndi a Mutharika sakukondwa nazo zina mwa nkhanizi.

 

 

 

 

Share.

317 Comments

 1. koma bambo chakwera nangangati mukunyanya inuyo enawa apanga bwanji? kodi ndinu mtsogoleri wa anthu otsutsaa kapena onyanyala?Nanga mukonza bwanji zolakwika?Chonde khalani wachitsanzo chabwino odziwa kupilira.Munthu wamphongo sanyanyalazinthu amakhala pompo kukambilana zimatha.

 2. most people here are just commenting without following the news that is going on. what opposition are doing is really helpful as far as democracy is concern. how can someone be a president by having 36% of the total voters. what opposition are pushing is a 50 1%
  Government promised the August House that the bill is going to be discussed in November and it is not listed to be discussed. So it seems Government is not doing what it promised the House thus why you see opposition doing like that. in summary it simply shows that Dpp is afraid of this Bill. What are they afraid of? Malawi yambani kupenya osamagona masanasana .

 3. Foolish comments against Chakwera are as a result of not following this link, find out first y they are threatening to boycott. Umbuli kumalawi nde vuto

 4. Zonyanyalanyanyala sanayambe lero mkuluyu anayamba kunyanyala za chipembezo kuyamba za ndale pano ndi uyu wanyanyala Parliament mwina akuganiza zokayamba za mpira athera moyenda mkuluyu.

 5. People are taking this as kunyanyala kopanda nako phindu and its your opinion,,zoti ndi M’busa sizikugwirizana coz Chilembwe analinso M’busa and tinamupatsaso Tsiku lomukumbukira M’busa John Chilembwe so za Ubusa muyambile 1900…

  It’s not easy for others to accept and understand the necessity to change, but we need to know our country is still going under democratic process interms of governance. That’s why we need to take a serious change of our electoral process….

  I feel we can develop because people will have the power and none will steal it from them Koma chifukwa cha anthu oganiza mwawo mwawo mosamvetsa kuti ndi chani do not see the substance in his boycott may be until the electoral process has passed mwina adzazindikira kuti

  WE WERE NEVER DEMOCRATIC TILL 1994 when change came

 6. I don’t think 50+1 olo atapanga pass ingatheke, coz zipani zikuposa number of districts in Malawi. Nd we shall be voting for second time pa zipani zomwe zizakhale pa competition that time as in kenya

 7. Amalawife,mavuto tidakalinawo,chifuka chilungamochimawonekelatu koma chimaphimbidwa,chifukwa cha ndrama owinamavoti,anali chakwela,koma tawonani lelo,asusamo oweluza,aweluza akutulusa,misozi akuziwa chilungamo,kuti nchelewaana awo apezakale,ovutika ndi amalawi,ambili ndiye ngati akukana achakwela,sakulakwisa boza la achikulilewo,liwonekelebe poyela

 8. Table 50+1 bill! Is it another that ATI? Ehhhhh! a Malawi, let us show we are civilized, ever time, things upside down, can’t learn from the recent bye-elections results, people spoke against impunity and we are not learning, hu!

 9. Kma chakwela nditcito yakedi imenei mot anthufe titakhala ambili wamaganizo ngat, WEL DONE NGULUBE aaaa ndithu zinthu zikanasinthad kma pot wannthu tilipo pangapo wamitima yosiyanasiyana ai ngakhale yesu akuuza ophuzila ake wenaso odalipo otsitsa okaikitsa ndpo mcifukwa cake akawauza kti ONE DAY… ONE OF YOU WILL BETRAY ME. so muganiza kti uleka ubusa ndie kti nditcimo pakut mulungu anakonda dziko lapas kotelo anampatsa mwanawake obwadwa ekha kti yese okukhulupilila iye akhalinao moyo osatha ndie anthunu anthufe tien tiziganiza komwe tacokela ndkimene tikupita osat umatukwana kunyoza bt was not gd at all tien tithandizane kti kod zafikapa tipangenazo motani osat umatukwana zipindula cian amalawi???

 10. Bakili Muluzi, Munthu wa ulemu kwambiri, Enawa shaaaa aonjeza, munthu wosusana ndi Yehova sangapange cha nzeru koma kunyanyala basi. Mumvetsetseni, just in two weeks mutu unandikula, but now i know where Chakwera is going…..

 11. Man chakwela apandiye sakuwonetsera kuti ndimunthu wanzeru,mukamva kuti ndinu wosunsa mudzingosutsa basi.Chokani kundale mubwelere ku um’busa,ndiyambisa mpingu wanga mukhale tsogoleri.L.Banda alikuti? taphunzitseni ndale munthuyu.Sindilimbali ya muthalika koma apa wandionjenza,akuyang’ana zake tsopano.

 12. Padziko lapansi kulibe ndipo sikudzapezeka munthu wabwino,inu amene mukunyoza Dr Lazulus McCarthy Chikwera atangokupatsani udindowu Kodi mungasinthe zinthu? Kodi inuyo mumati ndinu odziwa zinthu bwanji nanga osawauza zochita Dr Lazulus Chakwera.Achewa amati,mkadakhala ine adang’amba ng’oma.

  • Ndiye zimene akupanga achakwerazo zimenezo, akufuna kulamula nthawi isanakwane, angawaphunzitse anthu kunyanyala? Mesa amakambilana nkumapeza mfundo zomveka bwino amanyanyala? Olo a JZU Tembo ankapanga zimenezo??

 13. leader of opposition amayenera azikhara okura ntima kumene boma limampasa ulemu not watulo amakutora mukundaura kunyanyara kkkk mufunse malema ku south africa every day ndeu mu parliament , so ur complain wat , lack of education u guyz

 14. Let them walk out and leave those fat allowances. If one walks out after pocketing allowances then an injunction will be served to them.

 15. Koma Lazalo Chakwela ndiomvetsa chisoni. Chikhalireni leader of opposition anatsutsapo za nzeru koma? John Tembo and old MCP anaononga chipani. You don’t entrust such kind of leadership in hands of somebody who is not a good conversationalist. Chakwela is a coward. Kunyanyala kuthandiza chani pachitukuko cha dziko lino?? Akamfunse Joyce Banda m’mene anavutikila ndi DPP ikutsutsa. Akanakhala iyeyo atanyanyala dziko kumapita kwao ndithu. Mxxiii

 16. Kkkkk koma zina ukanva anthuni!, nde mukufuna aMalawi azavotere osogolera anzake kunyanyalayu? Chakwera ndimawana gyz boma sangaendetse alibe nphatso yausogoleri he is lk an empty tin, he don’t know wat to do, how n when to do it. Mark my words hon. Chakwera 2019 chanu palibe mukawafutse aTembo adazichitaposo zomwe mukuoangaz. Amalawi ngochenjera koopsa, take extra care!

 17. Chomwe ndidaonapo ine amalawi tilindivuto,timalephera kupanga chiganizo patokha n sitidziwa chomwe tikulankhula komaso kuzindikira komwe tikuchokera ndikomwe tikulowera.Ambiri mwa ife timangotsatira anzathu akalemba ma comment onyoza tonse timayambaso kunyoza mmalo mopeleka maganizo athu pankhaniyo ndibwino kukhala chete kapena kufusa ngat nkhaniyo sitkuimvetsa bwino kotero tithakumapeleka maganizo othandiza not kunyoza coz ngakhale timanyozana eni onyozedwa alibe nthawi yowerenga manyozedwe akowo kut mwina mkuyamikiridwa insteated tizipatsana maganizo as ayouth here in pages,Chakwera ndiotsutsa ndintchito yake kutsutsa ku parliament ngat sakugwilizananazo n sangaimbidwe mlandu komaso nkhan akunyanyalayi ndinkhan yapakanthawi kufuna kusintha ndondomeko yakayendesedwe kazisankho ndiyokomeya amalawi tonse osati chakwera yekha ayi,Ngat zinthu zidalibwino pazisankho za 2014 nanga boma likukaniranji kubweresa bill yi mparliament?Kod prezdent amamulumbilitsa usiku ndizoyenera kutero pamene lamulo limeneli tilibe?

 18. politics,, my foot! ever since I was a child, iv been hearing same old political songs but nothing is changing for a better,, and now m expecting grey hair to appear in my head but still more things are getting worse. Infact,, will not vote for anybody this time around. Thank God for the energy and power he gave to Malawians for they work so hard on their own and that they live at least better even though citizens produce are being robbed by these so called politicians. Mulungu sataya wake,, alinafe nganganga.

 19. Kma musamanyoze musanamve.nkhani yavuta chakwela ndi otsutsa nde mudziwe kut ngati wanyanyala zomwe iye amafuna sizikutheka. Boma la petulo mwaliiwala kod? Kut limamva zake zokha. Or ku south africa ngat sananvane D A Eff ndi ena amanyanyala kumene. Tsono chakwela akufuna kulongosola zinthu inu bas kumangonyoza. Simuziwa kut chilungamo ndi chipongwe

 20. It’s not the best way these is a Country working together we can do more to develop our nation whereever your rulling or opposition these Country it’s for us and whereever your DPP,MCP,PP,UDf we are one with one motive to develop these our beautiful MCP becareful people are watching u

 21. 50plus 1 muno ndiyosatheka muli zipani zoposa 50 kale ndiye ovota azivota bwanji kkkkk mapeto ake kuzikhala zisankho zachibwereza kungoononga ndalama, Mcp yazungulira mutu ndizisankho zamakhansala zathazi mukuona kuti pa udindo wa u president mcp siingawine nde mwati mulowere ku 50plus 1 hahaha Koma ndaseka, chisankho ndi anthu,,ena amavotere Mp wa chipani chosiyana ndicha president ndekuti mukuti anthu azivota bwanji

 22. That’s evidence that DPP is the party of Great vision,,,,, always DPP ikakhala m’boma imakumana m’mavuto,,,, this broaden the minds of the leaders.,,,, expect something great to come out after these problems,,,,, mind you, the best & suitable food 4. The brain is a problem,,,,,,! The only problem I see on chakwera is that,,, he is not tolerant,,,,, too much talkative

  • To u kachikopa, will 50 + bring development to the nation? Dont b fooled by ur chakwera. Since he attained his seat in parliament, what developmental measures has he contributed so far? What ne knows is to oppose. Kumangoweweta basi, eee apresident apa alephera, iiii koma boma izi zawakanika. Tanenanitu kuti mavutowa tingathane nawo bwanji 0/10. Onse amene ali ku legislature anasankhidwa ncholinga choti athandize kutukula dziko lathu. Kunyanyala nde kulepherako. Malawians need development.

  • A. Kachikopa. Ndi a president anuwo Ndi nthawi yoti muzipanga outline zomwe mukufuna kuzachita mukazalanda boma osamangoti mfwemfwemfwe Ndi ng’ona party yanuyo,,, mwamva.,,,, chipani cha nyaucho kkkkkkkkkkkkk

 23. 50+1, a DPP mukuiwopa? vomelezani kuti mukambirane bill yosintha ndondome ya chisankho kuti mukawina zikhale zovomelezeka ndi anthu onse azipani zosusa pezani njira ina yothesera kusamva kupatula zonyanyalazo

 24. Game a DPP yakulira..kaya asewera 90min + 5min yowonjera..mpilirawu uli 6-1..komabe MCP ikubwera wave after wave..uyu mmati ndani uyu..aah! ndayiwala ..CHAPONDA defender wangogwa..Dausi ndi KUSAYIRA midfield yavuta..kutsogolo nako kwabutha wochinya uyu..pitala waleka kale kale kutimwetsa wamkaka..MCP yangubweretsa timaplaye tachisodzera kutsogolo kuli waluso wodziwa kukhethemula njomba paja mmati ndani kodi chakwera..ee abale ..ATUPELE MULUZI WANGO CHINYITSA ALI PHEE!.achina ulemu,sosten,mia ndi sitolo ayivinitsa gule wakazukuta dpp..it never rains but it pours..kuno ku malawi zithu zavuta..kumagona mudima kutabwera alendo..

 25. Why walkout? Hw wl u say wht u thnk is right? Its tym u ppl grw up n build ths country, dnt b childish. Ur job is nt jst to oppose bt gv positive inputs for betterment of Malawi. If u nt careful u wont win

 26. Chisilu Niamene Akavotele Dpp Ineyo Nimapeleka Nsonkho Wokwana K5000 Pamwezi Koma Mwana MWana Wanga Akadwala Mankwala Sapezeka Kuchipatala Chaboma Msonkho Wangawo Ukulowa Muchithumba Cha MUTHALIKA CHILIMA CHAPONDA KASAILA DAUSI KALIYATI NI Nduna Nzonse ZA PETULO Wanuyo

 27. Ohh!!! if Mr Chakwera is showing this character with 5-1 how about if he wins? we will be in hot soop I tell u pple. True that a lion bares a lion.

 28. A chakwela ndimunthu omvesa chisoni kwambili maka potengela kuti ndimunthu yemwe saziwa chomwe ali ndip samamakhulupililabe mpaka pano kuti akulamulila mcp

  • Inagwetsedwa bwanji pa 17 October paja? Umbuliwu ukuvutani ndi evil dpp yanuyo, real Malawians are for Chakwera and mumva kuwawa simunati, ngati ndi mabanzi a cashgate akusokonezani mutu ndiye munsanza because real Malawians akumva kuwawa muulamulilo wa your evil satanic dpp

  • Hope chakwera akazawina zithu ndikuyamba kusalongosoka azakhalaso evil satanic mcp reader coz palibe amakhala president osapezeka kumalo kumenekuja kumachitika evil kuja ndie say watever makes u fil gud binniwell kachikopa

 29. This is one of the reason that will make me not voting 2019,i dont see the difference neither the benefits of voting.Am still sleeping on a mat,going to bed with empty stomach,on the same thatched house.Drinking dirty water no hope for the poor.
  Blessed are those pple ,selected by God that they wont participate on the deriberations of parliament procedings but at the end of a day they will pocket huge allowances,receiving full salaries haaaaa Dziko is not for the poor indeed but the reach.

  • you dont know what you are talking about,if you hv bread and butter on your table dont think the rest hv it.Go round on your villeges see how pple are struggling with life my dear friends.

  • guys, be serious. Enanu mukayenda nkuchoka kunyumba kwanu, wa ku office kapena ku business zanu. I am not speaking about myself here, but for the people in the areas you dont even wish to work in. there is real poverty in this country not that you see on the streets of fake beggars. people are living with absolutely nothing to call food, shelter or clothing. have some time and go to the remortest part of the city you live in. its not that they are lazy. they have land to cultivate, and they do. but with no fertilizer. they manage to harvest little and try to sell some for other needs. what do you people do? you send your goons in the name of buyers and rob them of their produce through buying at the cheapest prices possible. when they have nothing left to sell, or to eat, you start calling them lazy and ignorant. do you see such people getting better someday? what could be the reason for such people to vote, when all they get is this poverty? all in the name of politics.

  • Thanks mr Botha,these pple hv never been in such state thats why they are speaking like this.if the tin of maize is as cheap as per wat u hv said do u think one could roast it and eat everyday?Lord hv mercy on u pple.

 30. Koma chakwera mwina simudziwa kusutsa kwake nkopanda nzeru with no benefit becauz tikati kusutsa sitidati kunyoza ayi! komanso wosama demander zinthu zoti munthu ukuziwa kuti MW lero ndirero singapange ayi! kuwolokera ntchito ya anthu chakwera akukhala ngati wa ACB/ wa Police who is he it means udindo wake sakuwudziwa kodi ku Mcp ko kulibe wina wanzeru? awatu akufuna tiwone kuperewera nzeru kwawo asanakhale mtsogoleri! miseche too much that guy!

  • U have spoken well, u said Chakwera is like ACB or Police, that means he is the true son of Malawi. He knows that Malawians r in trouble with the big tareted idiot APM

  • Yes whether u like or not but our opposition in Malawi is a foolish! cauz he don’t know his responsbility! akakhala mavuto/umphawi ndiwakale ku Malawi ask ur grandparents! we keep on blame Mutharika no! ndi tulo tanuto khalani choncho but 4 those who knows the trueth chakwera ndiwopusabe!

 31. A MCP asananyanyale awerengenso chigamulo cha mulandu Wa Press Trust Reconstruction Bill
  Ambirinu munali muli ana kapenanso musanabadwe.

 32. Zingowonetseratu kuti Chakwera nzeru zake ndi zochepa, chifukwa iye yemweyu akumakhala ngati akufuna kunthandiza dziko. Koma nanga izi ndi chiyaninso, ngati mutayambe kunyanyala chimene chiwapindulire anthu ndichiyani? Nthawi ija mulikunja musanakalowe ku paliamentko, mumalankhula ngati wanzeru anthu amakudalirani kuti awa atinthandiza koma nanga izi ndichiyaninso? Malo moliwuza boma kuti mwalephera kunthandiza wanthu, ndiye apa mukuliwuza dziko kuti mukufuna kunyanyala kungowonetseratu kuti nzeru mulibe. Ngakhale, 2019 kuzakuvoterani nanunso anthu azakhala kulira basi. Ndiyensotu munyanyale malawasiwo, musangonyanyala zokambilanazokhazo.

  • A Jafaliii! Ochepa nzeru ndi Atupele ndi dull professor wanuyu, Chakwera is for real Malawians amene tikumva kupweteka ndi umbuli wa evil dpp yanuyo. Mark my words, come 2019 real Malawians are for Chakwera no matter what and mumva kuwawa simunati because truth pains and always prevail

  • Iye ndi otsutsa tsono ngati sakumvan nde mumati atani mumafuna mpaka amenyane. Chakwela sakulakwa or ku rsa ngati sakugwilizana munyumba ya malamulo otsutsa amanyanyala kuzolowela kulankhula ngat ndinu ochenjela pomwe muli odontha ngat petulo hiya

  • Ndiye ukhaula nayetu, chifukwa iye ndiye akulamula mpaka 2019 ukachitanso masewera ndi Bomanso mpaka 2024. Iweyonso kukamuvotera kawiri, wakuuzatu kuti sanakalambe adakali mnyamata chita masewera akowo ulira naye ameneyo. Umadziwanso munthu akakhala pampando umenewo, kumuchotsa simasewera ayi ameneyo amalizadi ma period ake onse Chakwera wakoyo akulira. Umufunse J.Z. Tembo, anaulilira mpando umenewo tsitsi loyera lisanayambe mutu mpaka lathamo tsitsi m’mutu akuulakalaka. Iwe amenenso mawa lomweli, utembenuka uyamba kumusapotanso Peter.

 33. Achakwera kunyanyala si nkhani even nthawi imene adali mwana amalonda kunyanyala nsima akayambana ndi munthu. Mchifukwa adanyanyalanso ubusa mkulowa ndale. Mutu mwawo nthawi zambiri suyenda bwino.

  • Umbuli wanuwo musamanamizire Bible quoting, Chakwera is real and backward never forward ever, inu tapitilizani ndi dull professor wanuyo tikuwonerani mmene zikuthereni because Chakwera is for real Malawians

  • Tizangoona akazawina chakwera 2019 kuti Mulungu anamuitanira ku utsogoleri wa dzikodi kumchotsa ku utsogoleri wauzimu that wil be seen in 2019 when he wins 🙏🙏

 34. ambiri ndinu mburi zophunzira ,sichakwera amene adauza amalawi eni Dziko kuti mu November abweretsa zankhaniyi.pano Ka 6 – o, mwadwala nako.anthu amene mumakana zipani zambiri ndinu mukutukwana chakwera.kodi pitalayo mumamutenga ngati Mwana wa mulungu,siyani kuopa kavalo wanu amalawi.

 35. komatu chakwela ngati ili misala ndiye avula ndithu kunali tu Tohn Ungapake Tembo akuti S 65 No 1 and Budget no 2 tiyeni kutabwela chisankho zomwe zinachitika ndikhulupila wina aliyense adaona zomwe amalawi adachita ndipo anayankhula osati pa fb koma pa movoti tiyeni tizingoyangana kuti zitha bwa

  • mmmmmm iwe Gama ingokhala chete ku mcp ndiye kulibe mafias ukunenao Pac yakenso ndiye iti ukunenayo yomwe inaxaza ndi mcp yo umaona ngati ife sitimaziwa

  • Mumva kuwawa zenizeni Chakera is real and for real Malawians not your dull professor who even fails to understand the basic economy and fails in everything, truth pains and mulira simunati. Tikufuna chilungamo osati macashgate anuwo, go yo hell with your evil fail dpp and dull professor

 36. mkukhala kwao awa, ali kuubusa ankakondanso kunyanyala nthawi zonse amanyanyala mzosadabwisa mkhalidwe lao kuwasogolela ana kuti aziziwa kunyanyala ndiye abusa amvula za zino ameneo

 37. 50+1 yikufunikilaɗi…angopeza solution yina rather than kunyanyala…i personally woulɗ like to see that ɓill pass!president asamalowe ku state house with 38% of the votes…at least he has to go into office with majority votes..of 50 +1

 38. ndiye choncho akazawinamo anthu akazayamba kumunyoza, kumugemula azatinyanyalansotu uyu ,zamugundika chakwela vuto anthunu mwamukweza muntengo wa papaya that’s why akuzimva kwambir komanso akuchita Boh kut khalidwe lo tizilionelatu

  • Kachikopa fool ndiiweyo,ngati ulipambuyo pachakwera usaganize kuti nditonse,choti udxiwe nkhani imene akunyanyalirayo njokhudza andale 50+ siikutikhudza pamene budget yo njatonse amalawi ndiye sitingasekelere zofoirazo kt wina akwaniritse zokhumba zake

  • Zomalumbiritsa President ku court usiku i think sichinthu choenera, Ndidalimva boma la dpp kt bill imeney aikambirana november, so hw cme kt alephere kuibweretsa? tinene kt amalawife timakondwera zinthu zizichitika mosaenera? kulira kwa malemu mbendera kunadabwitsa amalawi ochuluka kulumbiritsa usiku presdnt ku court nd chimene amalawi tinadabwa nacho,so to end this nonsese abweretse 50+1 ku parliament simple.

  • Which budget Chipiliro Chiluzi? And is budget an excuse to ran away from important bills like electoral reform? Or you even dont know what that electoral reform is? Arguing or debating for the sake of debating or because you benefitted from cashgate will never defeat the truth. Most Malawians are at pains today because of poor decision making of your evil dpp and its corrupt leaders. We need a president chosen on the basis of 50 +1 not 36%, 50 + 1 or any political process affects everyone whether wandale or not. Dpp has very selfish leaders, highly corrupt, egocentric and nepotistic, people are tired of it and real Malawians cannot go for this your dpp, mark my words come 2019, dpp will be booted out. Tikudziwa kuti mulimbalimba but where truth stands it always prevail. How can you improve macroeconomic conditions without improving micro economic condition? Your failed leader Mutharikas recent speech was rising above macroeconomic stability yet our microeconomic situation is down? Those that have subjective poverty like you chipiliro chiluzi and your fail clueless and directionless dpp cadets cant see the sense in Chakwera points, reread Chakweras speech and compare it with you failed leader speech. TRUTH ALWAYS PREVAIL, LOVE OR HATE IT

  • Ireen koma muja inalili nkhani yachimanga lero akhale oipa ndi Malunga?Even me,I support Malunga ndipo adagwira ntchito mokonda dziko lino

  • Zoonadi Akachikopa,mabill omwe adasiidwao ndiofunikiraxo kwambiri pofuna kukoza malawi wabwino,ACHAKWERA akunyanyala pofunika kunyanyalidwa,mabill enawo akawaikapo pandandandawo otsutsa abwereraso mnyumbai.

  • I reen , Malawi is in a democratic transitional process and I see we can do better kuti zikomele aliyense pa Malawi pano….kunyanyala kwa munthu uyu nkofuna chilungamo cha a Malawi chiziwoneka osati mokuba.

   Kaya anyanyala kaya atani inuyo mayi ndinu nzika ya dziko lino and zamalamulo mukuyenera muzidziwe let change come as it came in 1994 not focusing on a simple gesture yonyanyala yet mukukanika kuwona reason behind the movement

   By the way it’s not kunyanyala but movement

 39. Mumuuse chakwerayo kuti machende ake.

  Pa udindo wake palibe chikuoneka kuzintha. Amene akakwanitsa kusuza ndi tembo yemwe uja basi.

  Amene uja amaimiladi anthu ovutika.

  Osati za lerozi.

  Mzuru ndi mzeru panyini bas??

  • Koma chakwera guyz mwina simukudziwa kutsutsa kwake nkopanda nzeru ndi kwa no benefit a Malawi sitikufuna kutsatsa kwa mapokoso/ konyoza kodi a Tembo ankatero? sikuti muziswa malamulo iyemweyo wotsutsa koma akugwira ntchito ngati wa ACB/ wa Police who is he chakwera?

  • Yusuf ndi mwitha tafotokozani chimene watsutsa pamenepa inuyo mukuti amamgokhalira kutsutsa ndipo zimatheka bwanji kuti chakachilichose bajati yaboma amayiveza mnyumba yamalamulo ndipo sindingavepo kuti ayikana.

  • Ndizimene ndikunenanzo mbuzi iyiyi ilibe phindu lililotse.

   Ingobwerera mkachizi.

   Ndipo ndie imandinyaza koopsa.

   Ndine mwamuna koma. Ndikuti mundiuzire kwaiyeyo chakwerayo kt mapazi ake ..

   Kumalawi kwachuluka mitembo. Wamoyo ndi peter ekha.

   Osuza maliro.
   Mzika zap mzikomo.
   Maliro.

   Yonse mitembo yokha yokha.

   Mchifukwa chake kumalawi utsogoleri akamalamulira munthu wakwa amereca amapanga zoti ine ndiobwera.

   Ndipange business yi
   Ndikhapindura ndizipita.
   Kwathu.

   Machende anu.

   Maforena nonse including chakwera.

   Chinziru chamunthu.

   Mbuzi eni eni.

   Kwanu ndikuti chakwera iwe mapwara akho

  • kkkkkkk koma yaaa kumalawi kumeneko! ndye wabwino ndan? mwati olamula mbuzi zamapwala kukamwa otsutsa anamachende? mmmm apa ndiye che yusufu akalipadi ok zikavuta zedi ingosamukan mumulondole jb

  • Ngati mukufuna zoyambana ndie tiyeni.

   Cd chakwera or peter si ambuye anu mwamva agulugunyinda inu.

   Sizakuwaweni ngati kt ndakukwana abambo anu machende anu nonse
   mukulimbana ndiine.

   Ngati mukuona kulakwika osandipeza ku in box bwa. ???

   Kubadwa mopuza eti.

   Ndilibe chipani ine ndipo sindisazapota chipani mpaka kutsogoloku.

   Kwathu ndiku mocambique.

   Ndimangomva chisoni ndiubulutu umene uli kumalawi.

  • kungogwira kaganyu ndikupita ku shop kukagura ka fn ka itel mwati muxipereka malangizo pa Fb kuoneza kuzindikira???

   pa mtumbo panu.

   muziona ndi anthu ake.

   osati ine.

   muli ndichani agulugunyinda inu.

   kuchipanda zipani za mcp,udf,pp,dpp,bwenzi muli ndani??

   ana opuza.

   kulowa mnyumba mwanu kupeza ma ticheti azipani zonse.
   mcp,udf,pp,dpp.

   atidye nao.

   opanda chipani cheni cheni.

   mbuzi zawandu.

   kumutukwana chakwera mukakhuzidwe??

   nanga munakandiona ndi maso ndie munakandipanga zotani???

   ngati mukusowa mtendere apapa.

   anthu odya zachipani samasowai.

  • Yusuf idont doubt you are coming from vitsilu family and including your grandparents. Komaso nukhulupira kuti ndiwe mwana wa mchigololo.

 40. Kuganiza mopepela,zomwe mugwilizane pazokambilanapo ndizothandiza olamula okha??,Ochakwera mukufuna kulamula zikoli koma??.Mukamamva kuti kulozedwa ndiye kumeneku.Pitilizani tione mapeto ake.

 41. MBUZI YAMUNTHU, ANTHU ANAZOWELA KUNYANYALA MKUTE ALI ANG’ONO NDICHOMCHO. POMWE ANAKUSANKHANI NDI ANTHU IWE UKAMUNYANYALE MUNTHUWOTI AKULANDILA NDALAMA MWENZI NDI MWENZI POMWE MMALO MOKAMBILANA ZAKUPYA KUTI DZIKO LIYENDE BWINO.

  • Akanyanyala akuyenera kukabweza ndalama zomwe atenga ngati ma allowances opezekela Ku Parliament pa session imeneyi.Konzani zinthu osati kunyanyalako

  • BINWELL, MBUZI NDI MUNTHU AMENE ANASIYA KUTUMIKILA MULUNGU KUTHAMANGILA NDALE IWE SIUKUONAWEKHA KUTI CHAKWELA ANAPANGA UMBULI KWAMBILI??? YESU SANALOLEZE MUNTHU WA MULUNGU KUTENGA NAWO GAWO KU ZANDALE ZANDALE ZILI MUGULU LA KAISALA. NDICHIFUKWA CHACHE AMANGONYANYA ZILIZOSE. KUNYANYALA KOKHAKO KUMAWONO NGETSA CHUMA CHAMBILI M’BOMA KOMASO KWAPHELA UFULU ANTHU ZIKA ZA DZIKO. PAMAKHALA ZINTHU ZAMBILI ZOMWE ZIMAWONONGEKA M’DZIKO CHIFUKWA CHA WANDALE WOTSUTSA KUTSUTSA KOPUSA KOZUNZITSA WANTHU MZIKA ZA DZIKO. ANGAKHALE IYE ATATENGA DZIKO PADZAKHALASO OTSUTSA WENA AMENESO TCHITO YAWO NDIKULIKOKELA BOMA M’MBUYO UKU KUMAKHALA KUBWEZELA CHITUKUKO CHADZIKO M’MBUYO.

 42. who cares? That idiot is really irritating. That’s a sign of a loser. He will not make it. i domt want any reply but let me air oit my views…. MCP;Chewa people m tumbuka people are the ones behind our poverty.