COVID-19: Katemera okakamiza ayamba chaka chamawa
Boma kudzera ku unduna wa zaumoyo mogwirizana ndi komiti ya mtsogoleri wa dziko yotsogolera ntchito yolimbana ndi matenda a COVID-19, yati magulu ena a anthu ayamba kubayidwa katemera mokakamizidwa kuyambira January chaka chamawa. Izi ndi… ...