![Musician Jetu from Malawi](https://i0.wp.com/malawi24.com/wp-content/uploads/2024/01/Jetu-jpg.webp?resize=235%2C150&ssl=1)
Kunali kuphuluza chabe, Jetu apepesa potukwana
Woyimba Jetu yemwe anayika khwimbi la a Malawi m'botolo, wapepesa kamba kotukwana mukanema ina yatsopano. Kuyambira Lachisanu, anthu m’masamba amchezo akhala akugawana kanema wina yemwe akuonetsa woyimba wa zaka 72-yu ali ndi mdzukulu wake pomwe… ...