Bambo ndi mwana afa atadya chilazi
Anthu awili m'boma la Balaka afa atadya zomwe iwo amaganizira kuti ndi chilazi. Anthu omwe afawa ndi bambo wazaka 50 ndi mwana wake wa zaka 17. Izi zadza pamene athuwa amadya zikhawo chifukwa chanjala kamba… ...