Satana walephera – Chaponda
Anthu amene safunila a George Chaponda zabwino, anthu amene asanadye pemphero lawo limakhala lopempha Mulungu kuti mwina angozimitsa a Chaponda, ati ndi amene ankapanga upo ofuna kugwetsa a Chaponda koma alephera. Nduna yakale ya zaulimi… ...