Khalidwe ndi chuma: Gaba wanyanyula a Malawi
Nkhani yomwe ili mkamwamkamwa pa masamba a nchezo pakadali pano ndi ya osewera ku tsogolo mutimu ya dziko lino, Gabadinho Mhango yemwe lero watutumutsa anthu pomwe akuoneka kuti sanasangalatsidwe kuti anatulutsidwa m'masewero lero. Gaba yemwe… ...