
Kalisto Pasuwa wayamba kutumikira zofuna aMalawi
Mphunzitsi wa Flames yemwe wangolembedwa kumene Kalisto Pasuwa wayamba ntchito yake ndi chipambano pomwe wawaula Comoros 0-2 mu mpikisano wa African Nation Championship Qualifiers pa bwalo la Bingu mu nzinda wa Lilongwe. Zigoli za Binwell… ...