Alimi samalani: Bambo amunjata kamba kogulitsa feteleza wachinyengo
Apolisi ku Kasungu amanga a James Phiri a zaka 36 zakubadwa kamba kopezeka akugulitsa zinthu zonga ngati feteleza zomwe anazipakira m'matumba a feteleza ndikumagulitsa ngati feteleza. Mkuluyu wamangidwa dzulo kutsatira anthu ena omwe anatsina khutu… ...