A Uladi Mussa alowa MCP: Ati “Fotseki DPP”
Patangodutsa ma sabata ochepa chipani Cha Democratic Progressive Party DPP chitachotsa kamanso kuimika ena mwa ma Membala ake omwe m'modzi mwa iwo ndi a Uladi Mussa, iwo tsopano ati alowa chipani cha Malawi Congress ponena… ...