‘Ana anjoka inu’, Dorothy Shonga watopela omwe akumunyogodola za Zeze
M'modzi mwa anthu omwe ali mkamwa mkamwa pano Dorothy Shonga, wasambwadza anthu onse omwe akuti akumamunyogodola zokhudza ubwezi wake ndi oyimba Zeze Kingston, ndipo waulura atsikana ambiri ali ndi zibwezi zochuluka. Nkhaniyi ikutsatira kubwera poyera… ...