Ndalama za Covid-19: Wachiwiri kwa mkulu wa DODMA wanjatwa
Apolisi mumzinda wa Lilongwe anjata wachiwiri kwa mkulu wanthambi yowona za ngozi zogwa mwadzidzi a Fyawupi Mwafongo kaamba ka ndalama za mlili wa covid-19. Nkhaniyi ikutsatila kafukufuku yemwe akuchitika zitadziwika kuti ndalama zomwe zimayenera kugwira… ...