Zauchifwamba zitha kuchitika ku Malawi, boma la UK lachenjeza
Boma la United Kingdom lachenjeza kuti anthu ena ayesera kuchita zauchifwamba kuno ku Malawi. Mu uthenga wa pa intaneti, dzikoli lauza nzika zake kuti pali chiopsezo chokuti ziwawa zitha kuchitika ku Malawi. Langizio la zauchifwambazi… ...