Mankhwala a chifuwa chachikulu cha TB ndi aulere – atero adindo
Mpakana pano, anthu ena amaona ngati mankhwala amatenda a chifuwa chachikulu cha TB ndi ogulitsa zinthu zomwe adindo ati zakhala zikupangitsa ena mwa anthu odwala matendawa kuti asamalandire mankhwala mwandondomeko yoyenera komanso kusapita kolandira mankhwala… ...