Hule amugamula kuti akagwire ukaidi zaka ziwiri atatentha nyumba ya kasitomala wake
Khoti laling’ono la Chisenjere mu mzinda wa Blantyre lagamula mayi wina oyendayenda kuti akagwile ukaidi wa zaka ziwiri atapezeka olakwa pa mlandu otentha nyumba ya bambo wina. Khotili linamva kuti mayiyu, wa zaka makumi awiri… ...