Boma alipempha kuyikapo chidwi potukula masewero oyendetsa galimoto
Gulu la achinyamata omwe amachita masewero oyendetsa galimoto mochititsa kaso a motorsport-spinning pachizungu mumzinda wa Blantyre apempha boma kuti liyesetse kuyikapo chidwi pofuna kutukula masewerowa m'dziko muno ponena kuti ndiofunika kwambiri. Izi zanenedwa dzulo ku… ...