Malawi24

Afa atamwa osadyera

Njonda ziwiri ku Manja munzinda wa Blantyre, zabzala chinangwa kamba kochita chibwana cha mchombo lende kukonkha chakumwa choyankhulitsa chizungu ku mimba kukulira malikhwelu. Malingana ndi wofalitsa nkhani ku polisi ya Soche, Aaron Chilala, Vincent Chotokoma… ...