Apolisi asamutsidwa anamalira atatchingira nsewu mdipiti wa Chakwera
Patangodutsa maola ochepa pomwe anamalira anatchingira nsewu mdipiti wa galimoto za mtsogoleri wa dziko lino a Lazarus Chakwera mu nzinda wa Blantyre ndikuyamba kuyimba nyimbo zonyoza mtsogoleriyu, apolisi angapo amchigawo chakum'mwera asamutsidwa pa zifukwa zomwe… ...