Reggae sasungunula ngati Sobo – Jah Rhyno
Oyimba komanso kukanyanga nsambo mu chamba cha Reggea Jah Rhyno yemwe dzina lake lenileni ndi Hope Chiusiwa wa mugulu la Tuff Lions wati ayitanidwa kachiwiri ku kayimba ku Tanzania ku Zanzibar Festival mu August, chifukwa… ...