Mutale Mwanza wapulumuka pa ngozi ya pamsewu
Mutale Mwanza yemwe ndi wachikondi wa oyimba odziwika bwino m'dziko lino, Tay Grin, wapulumuka pa ngozi yomwe inachitika dzulo pa 20 December ku Zambia. Nkhani yonse ikuti munthawi yomwe ngoziyi imachitika, a Mutale Mwanza amayendera… ...