Photolab wayatsa moto pa Malawi
Kwatuluka zithunzi zam'nanu pa masamba anchezo zothyakulidwa muphika otchedwa Photolab; komatu zithunzi zina ukaziona munthu ukumapukusa mutu kuli kusamvetsa kuti nzanga uja ndi uyuyu? Atayela komaso kutchena mochititsa kaso. Photolab ndi apulikeshoni (application) ya mufuni… ...