Shingo “Haye haye” siwamisala – watsutsa Rick Pack yemwe amamuyang’anira
Makono ano masamba a mchezo akugwira ntchito yotamandika yofalitsa ma uthenga osiyanasiyana ngakhale kuti ena sawagwiritsa bwino ntchito. Pa matsamba amchezowa ena amawatenga ngati njira imodzi yochotsera nkhawa poti anthu ena amayika makanema osangalatsa ndinso… ...