Mgwirizano omwe tikufuna ndi oti Chilima akhale patsogolo – phungu wa UTM
M’modzi mwa aphungu anayi omwe chipani cha United Transformation Movement (UTM) chinapeza pa zisankho chaka chatha, wati akufuna kuti mgwirizano omwe chipani chawo chingalowe, mtsogoleri wawo a Saulos Chilima akhale pamwamba osati wachiwiriso. Izi zikutsatira… ...