Maso a amalawi ali tcheru ku bwalo la ndege la Kamuzu
Chichokereni mu nthaka ya dziko la Malawi mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika pamodzi ndi omutsatira pa 16 September chaka chino kupita ku United states of America, Maso a amalawi ali tcheru kufuna kumuonanso atamusowa.… ...