Govt. statement on Mutharika’s whereabouts raises questions


Peter Mutharika Ethiopia
Peter Mutharika Ethiopia
Mutharika is still in the US, according to Government.

The recent press statement from government on the whereabouts of the state President Peter Mutharika has raised questions with critics claiming that it has not addressed the serious questions that Malawians have on the whereabouts of their leader.

Government through its spokesperson Malison Ndau has released a statement to condemn Malawians who are spreading rumours that President Peter Mutharika is seriously ill in United States of America.

According to the statement which has been signed by minister of information Malison Ndau, President Mutharika is in good health and conducting official business in United States.

However, the statement appears to have unintended effect on Malawians as they have descended on it faulting it for not addressing the main issues that would allay the fears of Malawians.

Malison Ndau
Malison Ndau: APM is alive.

“Why isn’t the government disclosing the official business that Mutharika is doing in USA, why hasn’t the statement disclosed his dates of return?” a social commentator queried after government released the statement.

The statement has indeed failed to disclose the dates of return for the President simply indicating that government will announce his return dates as he is currently on official business in USA.

Another commentator wondered why government was threatening people with arrest for querying the whereabouts of their head of state.

“I used to think that all is well with Mutharika wherever he is hiding but the recent statement has made me think otherwise. Why is the government intimidating people who are wondering on the whereabouts of Mutharika?” queried another.

The Malawi leader left for the UNGA. Since the end of the summit, he has gone missing with reports indicating that he has fallen ill and has been hospitalised in USA.

 

259 thoughts on “Govt. statement on Mutharika’s whereabouts raises questions

 1. Moyo umadikila kumfa ndithu. Ndipo aliyese ali ndi tsiku lake. Imfa ya president sangawulutse thawi yomweyo ndi yomweyo ai. Coz pamayenera kukhala zinthu zingapo zoyenela kuti akozepo. Koma moto siwuyaka popanda ntchire chilipo chilipo ndithu chawavuta chebwana chigomingo munthalika. Tiyeni tichite phee atiwuza okha ngati ndi mpiru kut ampika adya. Paja amkulu wawo uja amkatelosotu nde mwina ndi style yawo yomwe amamenya.

 2. Ngat nzika zamalawi we have aright to where our president is and kuziwa zimene iyeyo akuchita tisamazangoona ma bill oti ankadwala pamene amalawi sitikuziwa please tell mtundu wa amalawi the truth

 3. Munthuyu Ndiye Wamwarira Ndithu But Aboma Akubisa,mwina Akufuna Abe Kaya Ndalama.

 4. i wish apresident athuwa akadalankhulana nafe nanga ngat mukuti sakudwala bwanji osabwela poyera ndikutiuza Kmanso a Malison Ndau ndi a Mgeme Kalilani Musaopseze mtundu Wa a Malawi Siifetu marefugee Ndife mzika zadziko Lino

 5. The truth will cam out .but we want to now if he still aliv or not .and wy you hid the truth? Something want wrong to Lpbrc of malawi .mukutinyasa mukamati muwamanga omwe akuti plz wakwatira.oloatafa mesandithawiyake.kapenandiwamuyaya

 6. thou inu aboma u want to hide da 2rth abt da president up to wen remmba maliro sabisa bt matenda amabisa tikukhulupilirani bwanj ñgat simumunena chilingamo n u r their kuopseza anthu,,does t mean president hviñg sam business meeting without malawiAn concerned yet he z using our tàx fees…mulibe manyaźi ndithu ..dyela limeñelo we vote 4 u kut mutithandiźe nt mutipatse mavuto …muzuzilanji miyoyo ya malawi ż dat a reason we vote 4 u..shame on u mukudyela pamutu anthu osauka iñstead ov helping dem..dziko lathu ndilosauka now źipatala zolipila kumachita olo evń muthu kukanika kugula chakudya nde muonà angakwanitse mankhwala.. remmba .mulungu alipo n akuona..

 7. Hello to everybody am very happy and glad to share this my wonderful and amazing testimony to the whole people of this world of the great work of DOCTOR dr sule an india doctor. This man is not a native doctor or a spiritual man, he is an herbal doctor that cure dangerous illness like; HIV/ AIDS,KIDNEY PROBLEM,HEART DISEASE,CANCER PROBLEM, and others dangerous illness which other english doctor has no solution to. The may reason why i am sharing this testimony is to tell the whole world that this india man DOCTOR //sule is here to help people who has that problem that are listed below.this india man is not a fraudter non a scammer because this man has help me and my wife after ten year of suffering from HIV/AIDS, he is a real good doctor, i and my wife was the one who told this DOCTOR //sule / to create an emai address because through this email he can help who has this problem. Truely this man is not a scammer he is a real doctor he is not here to eat money he is to help people because he has already help me and my wife. This india man has an email where you can contact. Pls d¶n’t play with this illness when you have it or someone around you. Contact he for he on his email address………. dr.sule via whatsaap +2348162447651

 8. Ngati ali bwino awuzeni azibwera tawasowa kuno komanso ngati akudwala get well soon komanso ngati amwalira RIP, palibe chobisika pa dziko lapansi ndipo tili okhuzidwa kamba koti kholo lathu sitikuziwa kuti ali kuti?

 9. kma a malawi tisadaule mwina mulungu pali chomwe waona mwayiyeyo palibe zomangana tinavote ndife ndiye chilungamo chyende ngat madz ndmoz mwa. anth amen asankhdwa kut akapume ifenso tikudikira ulendo wake omwewo nde palibe. chobitsa! tonsefe tikulira more dan u!

 10. we r all Malawians n he iz our presdent no matta what n let u the leaderz tell pple ov malaw who r chading tears waiting to hear the trueth! if u want still d money ov d govrnmnt den putting d trueth in public den y jst tellng d world knw d health status ov ouir prsdnt!

 11. Lets hold our mouth please! Lets not accept our mouth to control us! And lets rearn to have respect. Fear brings respect .am a oncerned citizen! Love you all

 12. Inu amene mukutokota kuti anthu asayankhule vuto ndichani or abomawo kuwauza anthu ngati iye akudwala ambiri akunena izi cos mu 2012 muja zinkateronso ndie enanu musadzionetse ngati kuti inu ndie odziwa mulunguyi

 13. Hello friends, am Juliet Phiri by name, i was one of those millions of people living with HIV, i received my breakthrough with the help of Dr Olumo whom i met through the testimony of someone he has helped, after some series of conversation with the person sharing the testimony i decided to contact Dr Olumo which i did, after some negotiation he sent me the medicine with an instruction on how to use it, i notice some change in my body when using the medicine, after completing the dose as instruct i went for test only to be confirm negative by the doctor after the result came out, words on the internet can not express it all, if you are in the same condition and you are looking for a way out of it you can contact Dr Olumo on his email address, [email protected], or you can call or whatsapp via +2348138956767.

 14. Peter is dead indeed. However Government is afraid of cash fraud as it happens after Bingus Death. All DPP vehicles are being impounded. Chilimas Security has been extended to that of President. The truth is that Peter z dead and he cant scroll back the watch. akumuchita kaye embam akamaliza anena

 15. If they are hiding information,obviously people will talk different things .Ma leaders a2 always hiding things ,Just approve the ‘ACCESS TO INFO BILL’ So that we shouldnt talk more hence we will kno th truth .Kumatiopsezaso tinakuvotelani tokha .Hahaha .Timangeni tonse tapanga comment za negative ndiyetu .Mumatichulukira nzeru ma tax athu omwe bwanji .Shupiti

 16. Galimoto yathuyi driver wasikamo , wangoisiya ikuyenda yokha ,kaya siyigwa? Conductor nayoso sakuonekaso bwinobwino. Conductor nayoso angoiyang’ana Galimoto, apa nde wakuphompho basi.

 17. Abale ndi Alongo musamatenge infa kukhala chinthu chopeputsa kwa ife omwe imfa sinatigwele pa mphuno, mwina kutheka timaiwonela infa ikagwa kwa Neba nchifukwa tikuyankula mosaganidza. koma ziwani kut pamene Yesu analandila uthenga wa infa ya Ladzalo adalila momvetsa chisoni, Nanga kuli bwanji ifeyo sitikukhunzidwa Infa????

 18. Eish koma anthu mumadziwa kuyankhula, akudziwa ndimulungu choonadi koma osanyodza kwambiri plz ngati amakulakwilani mungo nkhululuka siine wachipani sindimadzitsata koma musaonjeze ndimunthu wankulu tipeleke ulemu, kumakondana guyz udindo uwu ndiovuta zimaphweka zikakhala kwadzako dziko ili lili ndimavuto amburi olo mutznkhala inu simungalikwanitse bwanji kungozisiya mmanja mwamulungu ndiye oweludza.

 19. ProphetDr-Rex Kalolo: I saw a brain tumor that has caused major degree of paralysis. This will cause the incapacitation of great concern.my prophetic eyes can see this clearly. Pray my Malawi because God can do anything anytime.I am ready if given a chance to handle this and bring you best results

 20. Kunalembedwa; Life Is Shot And Tizafa Tonse, Moto Upita Kwasala Ntchire, Inuyo Ndi Aprofet Anuwo Muzalumphe Zenje Lamanda Ngati Muli Madolo Kuposa Yesu.

 21. Koma Ngati wafadi ndingoti ambuye alemekeze, death is something that u can’t celebrate but if this is true that mr ibu (peter) is dead and then for sure this will be worth to be celebrated

 22. Guys we all are aware of what our Government is good at when it comes to situations like this, just remember how long it took them to announce the death of our former Presidents Kamuzu and Bingu ,

 23. ABALE ZOLOSELANA IFA SI ZABWINO TIZIYAMBA TAGANILA KUTI NDILI INE AKUNENEDWA AGOGO ANU IWE UNGAMVE BWANJI MULI NDIKACHIPONGE ETI SIPAZAKHALA MSOGOLELI WABWINO KUMALAWI BASI

 24. ambuye wachifundo awalitse maso amalawi olankhula mopusa kumanyadila kufa kwanzawo ndikanakonda imfayi ikadagwera mabanja anu kuti enafe tidzanyadile ndi kulankhula bwino atamwale azibale anu ,imfa simphwando muzaziona

  1. Wow anthu ambiridi akutaya moyo kamba koxowa thandizo mzipatalamu nde ambiri avutike chifukwa cha munthu mmodzi yokhayo aaaaaa

 25. Guys anthu awa ndi ma cyborg, sanafe,Bingu nayonso payamba paja tinati wamwalira koma anadzatulukira ndipo anadzamwalira chika chinacho.

 26. Palibe chobisa apa, twuzen coz munthu anachka kufumbi azabwranxo ku fumbi. Ndy boma mpaka kuwopseza .also mabuku amanena kt aliyese azalawa ifa

 27. chonde a Malawi anzanga pasapezeke olira apa ayi ndipo yese akhetse msozi kamba ka Bwampini ndi MFITI ndithu coz munthuyu wakhaulitsa osati masewera uyu eish

  1. Chitsiru chamunthu iwe , chizete cheni cheni galu oganiza mopusa, do you think iweyo ndi wamuyaya suzailawa imfayo? uzaikidwa ngati galu aise ungodekha mbudzi ya munthu iwe mxiii

  2. Billy c Jali mwati eti kkkkkk tsogolo lako lathera pompatu mafana ozolowera kupatsidwa mwanya nayo kkkkkk mpaka kundiopseza kkkkk koma nde zooopsyatu lekani kudalira gwirani vepi ndimanja anuwo akhwirikhwiri inu ana anjoka…agong’oli…achabechabe inu to hell with bwampini wanuyo kkkkkk

 28. Umbuli unakula kwambili mu boma ilo anachuluka ndi atidye nao osati anthu ofuna kutukula ziko nde chilichonse angapange panopa ndichokhacho chopindulira iwo osati dziko.. Chikakhala kuti iwowo chodyapo palibe mchopindulira anthu mdziko amachikana.. Malawi will not grow guys unless government faces an overwhole.. Kuyamba kuzipani mpaka mu ma offices onse aboma pokhapo malawi azayambe kuoneka kusintha

 29. Umbuli unakula kwambili mu boma ilo anachuluka ndi atidye nao osati anthu ofuna kutukula ziko nde chilichonse angapange panopa ndichokhacho chopindulira iwo osati dziko.. Chikakhala kuti iwowo chodyapo palibe mchopindulira anthu mdziko amachikana.. Malawi will not grow guys unless government faces an overwhole.. Kuyamba kuzipani mpaka mu ma offices onse aboma pokhapo malawi azayambe kuoneka kusintha

 30. “Maliro sitibisa” is what my wife said this morning. If he is dead, the funeral will come home. They can’t hide that. It might be hid for a while but he will be buried here and so we will know the truth even amid government propaganda on this issue. “Time is the mother of all truth” another wiseman said. Asatiopsyeze awa for the rumours, izi aziyamba okha. If they told the truth, people wouldn’t be talking about it in the first place.

 31. kodi inuyo ngati muli atolankhani enieni osafufuza bwanji ndikutiwoza komwe ali mungoti phwiii kumatifusaso ife, mesa mati ndi atolankhani mangoziwa kutola nkhani zaboza basi mwatikwana musapositeso mwava mwixiii

 32. I can smell something fishy here, why is it that the Dpp administration is playing a game of hyd and seek? something…somehow..somewhere might have gone wrong……

 33. Apapalibemvuto president oloatabwele oloasabwelemsanga.palibecimene cingasithepoapa amalawi kwathundikulila kosatha bansi

 34. Inu mpaka kumatiopseza ngat tili mdziko laen,ife tileka unless mutakamba chlungamo bas.wafa kapena alimoyo? Nkhan yake ikhale yamafunso nd mayankho thats all

 35. That guy called peter is dead the goverment is hiding the truth.Ok if his is well why he is not speaking one word to malawian? Why is he hiding? It has been long now without seeing him talking to any media in USA. What meeting is he attending? Stop fooling malawians. stupit officials

 36. Anyongedwe basi ,mbuli kuzolowela kulima sabola ndekumati prsdt sali bwino kulibe chimanga kuyiwala kt munalima sabola

 37. Ngati munthu wasankha kukhala wandale kapena tsogoleri kumafunika upewe ka moyo kodziva komaso ka private chifukwa anthu sangakondwe kumakhala osadziwa komwe uli kapena ukutaniko koma moyo oipa ubwana supanga ndi ku dwala kapena ndi imfa sizoona tidxiva lero zina mawa zina nzanu dziko lina mupha ndi uyo wayankhayo nanga iweyo ndi ndani osanena bwanji ma google onsewa

 38. There Something Similar Between Zambia and Malawi. The Two Country share the Same Currency (Kwacha). President Mwanawasa died in office whilst attending the summit. when Mbingu wamutarika and Mwanawasa died, They were succeeded by two Vice president (Joyce Banda and Rupier Banda). They both Lost Lamentably to their main Opposition rivals. Could the speculations over Wamutarika’s demise true?. Since Zambia has Lost Two Sitting presidents, Can this happen to Malawi also. The answers Are with God the Creator. May the mighty God continue bless Malawi in this trying moment………. Greetings from Zambia

  1. what a good logic, certainly ithink malawi can also loose two presidents as well depending on the samples of the available data.

 39. Ngati sakudwala ndekuti akupanga za greencard,kutanthawuza kuti akufuna kukhalabe mzika ya America,ndekuti simmalawiso ameneyo.

 40. Dziko likufuna kuziwa chilungamo even bambo ngati sakubwera komwe anapita ana amafusa amayi kuti aziwe ndie nenani chilungamo kuti tiziwe basi ngati wamwalira siwoyamba kufwa anthu ena tikunena pano akulira maliro abale awo ifa ndi ifwa basi. Ngati ali moyo tingopemphera akhale ndi moyo wautali zikomo kumpando.

 41. Please die already, you’ve screwed us enough, its my prayer that the rumours should be true, if not i still pray that should come to pass, help us God

  1. Ngati dziko kuvomereza ndikomvuta akufufuna kuononga kaye chuma chaboma kaye komaso. kodi Ngati mtsogoreri wadziko angachoke mdziko lake kukakhara dziko kkkkkkk lanuwake mpaka 2moth he have problem but gavarment he doesn’t want to tel people in our country Rip

 42. the distance between egypt and israel is about 613 km. but it took moses and the israelites 40 years to complete their journey.on the average each day they walked only 43 mitres,yes 43 mitres almost half of what usain bolt does in 5 seconds. i just wish moses was around to explain this laziness……

  1. Atinkenawo ankamuvutitsa Mose modetsa nkhawa pokumbuka miphika ya nyama ndinso mavembe akwa Farao choncho ankatha xaka xaka ali malo amodzi kupanganso ulimi ndi zinandizina m’njila kupanga ana….

 43. Adadi akhalitsa ku america akulogosola kaye ziwiri zitatu akubwera musayembeke zingachitikxo za bingu never iam saing never

 44. If he is dead he is dead,nothing to hide,the father has abandorned his family,ndife nkhosa zopanda mbusa thus all. Kadzikokang’onong’ono kosauka koophsya ko,ma zochitika kuuuuu,i am tired.

 45. What is so difficult for the goverment to just tell the citizens who voted him the truth. If he is sick, everyone gets sick and they must just say it to avoid this rumours. Pple are now confused becoz no electricity, no president whereabout, no answers, no water, no food. Everything is just a mess.

  1. What michael is saying is true our president is no where to be seen so wat do u expect us to say .may be he is dead we want solid answers nat wat they are doing where is our leader thats the questiön nothing

  2. What michael is saying is true our president is no where to be seen so wat do u expect us to say .may be he is dead we want solid answers nat wat they are doing where is our leader thats the questiön nothing

  3. What stupid do u mean Nesta? Every country has a leader. And the leader has duty to do as a leader. We are facing lot of crisis and they are not attended. He is suppose to be here to intervene all this crisis as a leader. He is president of Malawi not America. I think Nesta u are the one who is losing mind here and showing maximum stupid. Why not just eat shut up.

  4. Come on Stamford. U went to school. Majority and minority i am sure you know what this means. When pple vote, the majority eat minority votes and that makes majority to be in power. And thats how we say Malawi voted APM to be their president including u and me who didn’t vote for Dpp. He is now President of Malawi by winning majority vote. It doesn’t matter u voted MCP, but u are been ruled by majority votes winners.

  5. I am a cool guy @ Clement. How can someone just call stupid without a reason. I am sure u understand that if a parent is away and at home they is lot of problems. And he cant give any answers why he is not at home. Then who is to blame for any crisis affecting family. He is supposed to be blamed for his absence if they is no where to be seen.

  6. #billy_jali tonse ndi ana amahule. iwe, ine ndi michael ukumunenayo ndi ena onse coz kuti tibadwe amayi athu amagonadi ndi amuna awo. so no need to call afrend THE SON OF BITCH. makolo sizikuwakhuza pano.

 46. wat z he stl duing thea??monga mavuto akunyumba kwake kuno sakuwaona 3 wikx kudziko la eni chikumusangalasa ndi nchan anthu sasiya kuyakhula antil amuone or anve mau ake

  1. Zoona komaso tamva kuti akuti anthu akayakhura zokhudza zayiyeyo adziwamanga koma ngati paufulu we have to talk intill to be back there in our country paufulu wanthu TIYAKHURA BASI.

 47. chilima alumbilisidwa liti?kodi manda paja anakumba kale ku ndata azangofikira kuyika chifukwa chakuti sitingawone nkhope muja ilili khope ndiwe wamwalira inu mungakhale ndi chilako lako choona mmmmm

 48. God am asking your favour to recover soon my beloved president peter munthalika,the one who i loss my sweat online queing to vote him,so if you planned to take his sour,let your will,bt if it from satanism please load am asking to show us your priority,o God of heaven heal my president if possible.Ameen

 49. I advise the government to inform the nation the true story about the president so that people can stop the speculations and prove them wrong

  1. If Government r failing 2 tell the Nation the truth about the whereabouts of the State President, there’s a Government in Malawi??

 50. 1bilion already spent, is this profitable stay, minus this amount how much more money will be added to benefit the citizens?????????

  1. Tiziza ona nkhope ngat amalawi namfuko wapita mpake anakalamba kkkkk akapume chilima woyee upresident wapixo pakati alomwe pezan chna chochita your so called bwafu is gone

  2. Tiziza ona nkhope ngat amalawi namfuko wapita mpake anakalamba kkkkk akapume chilima woyee upresident wapixo pakati alomwe pezan chna chochita your so called bwafu is gone

 51. pamenepo ndipo ife ambili amalawi tikufuna tiziwe but mumatiopseza zinthu zopanda ntchito shatup ife tikadi kukufusan mafuso ngati ameneo ngat anamwalila tizionela limoz tikayika ku ndata kwao kuja

Comments are closed.