Olo wina afune, asafune MCP ilowanso m’boma – atero aChakwera
Kaya ena akumalotabe nkumaganiza kuti adzachotsa chipani cha Malawi Congress m'boma, izi ayiwale kamba koti aChakwera akuti chipani chi chilowanso m'boma chaka cha m'mawa. A Chakwera amayankhula izi ku msonkhano waukukulu wa chipanichi ku Bingu… ...