A Chakwera akufuna kulanda Boma – atelo a DPP
A Lazarus Chakwera ndi kutheka anagonja pa zisankho mu 2014, koma a chipani cholamula cha DPP sakugona nawo tulo. Malinga ndi chikalata chimene chipani cholamula cha DPP chatulutsa, mtsogoleri wotsutsa bomayu ati ali pa kalikiliki… ...