Dalayivala wina waliyatsa liwiro nkusiya galimoto ndi matumba achamba atazindikira kuti payipa
Apolisi ya Nkhunga m'boma la Nkhotakota, akusakasaka dalayivala wina yemwe ananyamula chamba cha nkhaninkhani mu galimoto yomwe iye amayendetsa ndipo atazindikira kuti apolisi akumutsatira anayimika galimotoyo pa malo ena mkuliyatsa liwiro la mtondo odooka. Nkhani… ...