Chakwera anandisankha chifukwa ndimatha kupempha – watelo Usi
Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino Michael Usi wati iye anasankhidwa pa udindo wake ndi mtsogoleri wa dziko lino Lazarus Chakwera chifukwa choti iye ndi namatetule pankhani yopemphetsa kwa azungu. A Usi ayankhula izi ku… ...