Anthu atali atali amakhala pachiopsezo ku mphenzi, watelo katswiri wazanyengo
A Akimu Phiri, m'modzi wa akatswiri ku nthambi yoona za nyengo m'dziko lino, achenjeza anthu omwe ndi atali atali kuti akuyenera kumayenda mosamala maka munyengo ya mvula ponena akuti anthuwa amakhala pa chiopsezo chowombedwa ndi… ...