Namadingo aputa mavunkhomola
Oyimba odziwika bwino Patience Namadingo waputa mavunkhomola atanena kuti oyimba nzake Lulu sanafike mu gulu la oyimba otchukitsitsa komanso omwe sadzaiwalika mpaka kalekale m’dziko muno. A Namadingo ananena izi masiku apitawa pa tsamba la mchezo… ...