Sukulu za pulayimale zomwe ophunzira amuna akuvala ma buluku ngati yunifolomu azichenjeza
Sukulu za pulayimale za boma zomwe ophunzira ake amuna anayamba kale kuvala ma yunifolomu a ma buluku, zachenjezedwa ndi unduna wa maphunziro kuti zisiye ponena kuti pakadali pano lamuloli silinakhazikitsidwe. Chaka chatha, phungu wa nyumba… ...