Sitinagulitse nsika wa Kamba – yatsutsa khonsolo ya nzinda wa Blantyre
Khonsolo ya nzinda wa Blantyre yatsutsa mphekesera zomwe zikumveka kuti yagulitsa nsika wa Kamba kwa mponda matiki wina wa chimwenye. Sabata yomwe ikungothayi kwakhala kukumveka manong’onong’o kuti khonsolo ya nzinda wa Blantyre yagulitsa nsika wa… ...